Ndabalalika, ndabalalika
Oh! ndabalalika ndabalalika
Ndabalalika, ndabalalika ndabalalika
Mafuta akwela
Sopo wakwela
Ndiwo zakwela
Eish, zavuta
Mafuta akwela
Sugar wakwela
Rent yakwelanso
Ayi zavuta
Ndalama zanga ndipatse ndipatse
Ndalama zanga ndipatse ndipatse
Ndalama zanga ndipatse ndipatse
Ndalama zanga ndipatse ndipatse
Ndabalalika, ndabalalika
Oh! ndabalalika ndabalalika
Ndabalalika, ndabalalika ndabalalika
Mafuta akwela eish
Mafuta akwela
Rent yakwelanso ah ah ah
Mafuta akwela
Rent yakwelanso ah ah ah
Nndipatse ndipatse
Ndipatse ndipatse
Wangongole yanga ndipatse ndipatse
Ndipatse ndipatse
Поcмотреть все песни артиста
Sanatçının diğer albümleri