Loyal
Loyal hustle the factory
Heeeh
Ukali
Mwinamwake ndiyambe yogulitsa tomato
Iliyonse mwina mkukwaniritsa maloto
Moyo pano sukugawa kamba olo dontho
Kumayesa kuwopa kunong'oneza bondo
Ndikadekha ndimakhala nduganizira
Zambiri ntchito yanga ngati mamuna kuganiza
Kwambiri ndizipemphera
Kwambiri ndikapemphere kuphiri
Kapena ndiyambe kuba, ndikawabele a Phiri
Moyo wu umafuna torch
Kuwona kuwala kumafuna watching
Nthawi siyili mbali yathu ndika enemy
Tikuthamangitsana nayo mwa Tom and Jerry
Ndukufuna business ndipange bwanji panopa ndilibe capital
Ndipite John's Lilongwe yakwana panopa ndithawe capital
Ndimange nyumba
Ndimange banja
Ndigule benz
Ndiyambe kuba, ndiyambe geni
Ndivaye John's
Ndipeze ntchito
Ndiyambe geri
Ndipeze mbidzi
Mwana ya fees, chimanga chatha
Ndiyambe chiti, (kudya mutu)
Ndipange business, (kudya mutu)
Ndipange chani, (kudya mutu)
Ndivaye John's, (kudya mutu)
Ndipange plan, (kudya mutu)
Ndipange business, (kudya mutu)
Ndipange chani, (kudya mutu)
Ndivaye John's, (kudya mutu)
Ndipange plan, (kudya mutu)
Mukaona phee ati kufatsa, mukanadziwa
Ndimakhala ndikulingalira ndilowele pati, kuthawa usiwa
Kuguba daily ku huster, mwina ma net mwina masuki wa, (mwinawake et)
Ndimawamvetsetsa mafana angokhalita kudya ma usti wa, (napepe)
Kapena ine kubadwa ndi ngozi
Tsiku lililonse kusamba misozi
Popanda nzanga obwera ndi cross
Ndikazitolera andidyele a Rose
Ndilowele kunyanja kusanduka msodzi?
Kapena ndingogwira mwana waka Mfozi
Muthyolo mu mwina nditha kupata mgodi
Mkuzangofikira kukhala landlord
Ndimange nyumba
Ndimange baja
Ndigule benz
Ndiyambe kuba, ndiyambe geni
Ndivaye John's
Ndipeze ntchito
Ndiyambe geri
Ndipeze mbidzi
Mwana ya fees, chimanga chatha
Ndiyambe chiti, (kudya mutu)
Ndipange business, (kudya mutu)
Ndipange chani, (kudya mutu)
Ndivaye John's, (kudya mutu)
Ndipange plan, (kudya mutu)
Ndipange business, (kudya mutu)
Ndipange chani, (kudya mutu)
Ndivaye John's, (kudya mutu)
Ndipange plan, (kudya mutu)
Поcмотреть все песни артиста
Sanatçının diğer albümleri