Kishore Kumar Hits

Henry Czar - BBC şarkı sözleri

Sanatçı: Henry Czar

albüm: BBC


Heeeeh
A malawian rapper Henry Czar
Is no longer a member of Ukali Entertainment
As it stands it seems like they are not really doing songs together
Ok this is MBC, no BBC, no Al Jazeera, no aah
Anthuwa ndi oyipa samafina zidziyenda
Zako zikamayenda amabwera ndi chi blender
Kufuna kusokoneza akunyenye ngati mice meat
Kukujeda kumbali pamaso ngati amzako
Usandiyandikile ngati uli kazitape
Mfana ozikonda omana key rian mbappe
Malawi ndi jungle mwangodzadzana agwape
Osowa zochita busy kumangomwa mchape
Ati dollar zake zonse zija mesa mzakumidima
Osamakopeka nawo awo ngo nkhwima
Nanga mwanamwana ngati uyo mpaka bima
Samatseka kamwa amagojeda
Anthuwa BBC, BBC
Anthuwa BBC, BBC
Zodiak Times, MBC
Aj jazeera mkati, ABC
Koma mwamva
Mwana waneba watenga phaa
Mwamvaa
John pano anagwira Mphaaa
Mwamvaa
Anatha pano sizikuyenda
Mwamvaa
Zawo pano zili pendapenda
Business yawo inaduka
Pano anasawuka
Chithumwa chawo chinasuluka
Paja amkawuluka
Bola tinafanana
Tikanjoya kumwamba
Tikayimba hosanna
Hosanna hosanna hosanna
Ati dollar zake zonse zija mzakumidima
Osamakopeka nawo awo ngo nkhwima
Nanga mwanamwana ngati uyo mpaka bima
Samatseka kamwa amagojeda
Anthuwa BBC, BBC
Anthuwa BBC, BBC
Zodiak Times, MBC
Aj jazeera mkati, ABC
Anthuwa BBC, BBC
Anthuwa BBC, BBC
Zodiak Times, MBC
Aj jazeera mkati, ABC

Поcмотреть все песни артиста

Sanatçının diğer albümleri

Benzer Sanatçılar