Kishore Kumar Hits

Macelba - Ndifunsa şarkı sözleri

Sanatçı: Macelba

albüm: Ndifunsa


Uuuuuh
Ooh ooh!
Look
Dear admin
Dzulo ndinagona osaphaka
Sungandimvetse admin yeah
Dzana nali ndimafriends timayaka
Nkawauza ndudutsamo sandimvetsa
Bola nzingothokoza kuti anandimwetsa
Nine months pano ngini yanga yangoima
Ka hope kanga nkakango'no
Zizayenda mwina
Koma admin eh
Paden rent yanga njosasotha
Kupha nyerenyere anzanga akugula ma motha
Zingongole mbwee ndigwire mtengo wanji
Koma zikundivuta bwanji
Ndikatchena ngati ndilibe mavuto (mayoh!!)
Pandekha kusisima ndazazidwa ndimavuto
Am looking for an answer
Zikatere mumatani
Mundifunsire kugulu but please hide my ID
Mtima nde kufuna ufuna
Kufunsa nzeru Kwa anzanga ndi abale
Ndikudutsa muzambiri ine
Pandekha sinkwanitsa no
Komano nkhawa bii ine
Nkutheka ndinyozeka
But I will say it anyway so please
Hide my ID
Ndifunsa Ndifunsa ndifunsabe
But please Hide My ID
Ine mungondithandiza so please
Hide my ID
Ndikufuna nzeru zanuzo
Osati chitonzo chanucho ooh!
Yah Dear admin
Ndili osweka mtima
Sindikumvetsa admin
Kapena vuto ndine mwina
Ndikayesera kukonda zimangothera misonzi
Nazilakwira chani mphongozi
Mesa mmati zizakhala better
Kapena nalengedwa kuzafa mbeta
Wanga mamuna amveka bwanji mphete wina
Wanga mamuna wapereka pathupi kwina
Pressure ya anzanga afuna tonse tikwatire
Pressure ya amama zizukulu akumbatile
Ndikaphoda ngati ndilibe mavuto
Pandekha kusisima ndazizidwa ndi mavuto
Am looking for an answer zikatele munatani mundifunsire kugulu
But please hide my ID
Mtima nde kufuna ufuna
Kufunsa nzeru Kwa anzanga ndi abale
Ndikudutsa muzambiri ine
Pandekha sinkwanitsa no
Komano nkhawa bii ine
Nkutheka ndinyozeka
But I will say it anyway so please
Hide my ID
Ndifunsa Ndifunsa ndifunsabe
But please Hide My ID
Ine mungondithandiza so please
Hide my ID
Ndikufuna nzeru zanuzo
Osati chitonzo chanucho
Nkhawa njeee
Osadanda dzina ndiye sititchula
Koma yankho lenileni komanso lowona
Ndiye ndi ambuye basi
You've got a role to play
Muli ndi mbali yoti muchite
Ngati munthu muyanga'ne
M'mene muchitira zinthu zanu
Mwina mukumachita komabe
Pena osachita bwinobwino
Mwina kumasamba thupili
Mtima uli waumve zedi
Kutheka kumakankhadi zoona
Koma osadziwa komwe ukukankhila
You've got to balance
Muziwunguze
Mukachita mbali yanu
Kwinako timsiyire ambuyee
Hide my ID
Ndifunsa Ndifunsa ndifunsabe
But please Hide My ID
Ine mungondithandiza so please
Hide my ID
Ndikufuna nzeru zanuzo
Osati chitonzo chanucho

Поcмотреть все песни артиста

Sanatçının diğer albümleri

Benzer Sanatçılar