Kishore Kumar Hits

PiksyMw - Nzanga şarkı sözleri

Sanatçı: PiksyMw

albüm: MTUNDA


Nzanga ulibwanji?
Zikuyenda bwanji?
How is your family?
Business ikuyenda bwanji?
Poti dzikoli nde lavuta kwambiri
On a daily, tikuluza fanz
Kaya chaka chino zitithela bwanji
Everyday kugwada pansi
Mulungu akhululukire dziko la pansi
Please hold on, my friend
Stay strong, it's gonna be bumpy road
I have hope, my friend
We gonna be alright
Koma pompano tikumana
Tiyese kudzisamala
Posachedwa kuwala
Mwina tingodzisamala
Osaopa nzanga
Poti kukondwa ndi mawa
Pompano kuwala
We gonna dream of these days
I miss those trips to the lake
Zima boat ride uku tikusekelera
Achina DJ Crips on the deck
Tikuvina ndima cup tikumwe-mwelera
Koma wapita-pita-pita-pita
Tingosamalira mwina tidzawina
Ayi-ah, ayi-ah ayi-ah, ayi-ah
Tingosamalira mwina tidzawina
Koma pompano tikumana
Mwina tingodzisamala
Posachedwa kuwala
Tiyese kudzisamala
Osaopa nzanga
Poti kukondwa ndi mawa
Pompano kuwala
We gonna dream these days
Ayi-ah, ayi-ah ayi-ah, ayi-ah
Ayi-ah, ayi-ah ayi-ah, ayi-ah
Ayi-ah, ayi-ah ayi-ah, ayi-ah
Ayi-ah, ayi-ah ayi-ah, ayi-ah
Yes, I miss church
I miss family
I miss being in the gym
I miss hiking
I miss those shows
I miss you all
Please stay safe, my friends

Поcмотреть все песни артиста

Sanatçının diğer albümleri

Benzer Sanatçılar