Lucius Banda Atumwi A-Taps production tiye Anenani tabwelani Mutandiuza ndichani Atsikana ku Lilongwe andithetsatu makani Akumati akatchena Tidzikope aka twiser Ti mahip akamayenda Monga njoka ya mamba aaa aa aa Ndalephera kupilira ine Ndalephera kudzigwira ine Ndatchona ku Lilongwe ine (mayo) Ndikwatira ku Mitundu ine Ndikwatira kwa Kauma ine Ndatchona Kuchitedze ine Ine ndi utchona wanga Ndimagomera za kunja Osadziwa kumudziku akazi akutchena Ine Zulu woman Ndimuwuza adzipita Ndikufuna wa Malawi Wa nphini za chipole eee ee ee Ndalephera kupilira ine Ndalephera kudzigwira ine Ndatchona ku Lilongwe ine (mayo) Ndikwatira ku Mitundu ine Ndikwatira kwa Kauma ine Ndatchona Kuchitedze ine A Nthumwi let's go Nthumwi ndipatse space (space) Ndipatse space, why? Ndapeza tsuna mu Lilongwe ati imakhala mu Nchesi Mbina yokhayo ndi magetsi Thupi langa lonse kugwidwa nyesi Nane, ndangotiso male cha ukuku ku Kawale Ndimati ndikapatse mwana kenaka ndikathawe (koma) Koma nkomwya wake Ndiwo wandichela ndale Mutumize uthenga kukabowola kuti Nthumwi zatchona mu Lilongwe Mayi wanga Namoyo ng'ombe zija gulitsani Sindifuna kulowora ndapeza ku Likuni Amavina chintoli Amaponya ka sitepe Anaduka ka chiuono ka Ine mtima kusonthoka aaa aa aa Ndalephera kupilira ine (mayo) Ndalephera kudzigwira ine (mayo) Ndatchona ku Lilongwe ine (mayo, mayo) Ndikwatira ku Mitundu ine Ndikwatira kwa Kauma ine Ndatchona Kuchitedze ine Ma tsuna andizunguza apapa ndisankhe uti? Mulungu thandizeni osati ndisankhe njuchi Pachuluka atsikana, mtimamu muli kulimbana Kodi ntani ine? ndingolowelera Mwamuna mkabudula amathera moyenda wawa Tsono pafunika tsuna yoti idzimuchotsa nkhawa Iwe kumana eeh, kumana eeh Wandimana wandimana Chamba choyatsayatsa chamba Come sweet and gimme some brown sugar baby 'Cause when wind your body, you make me feel so dizzy Oh dizzy, dizzy that I don't know where to touch you Come move you body Just like a cobra Come paint your face Just like a princess I may go I kiss your lips and touch your body and make you feel the woman you are