(Yes it's manganye eh) (Sonye, Sonye wooh) Na na na na na Kodi ndi malodza Palipose pangonyelenyetsa pokha Usiku onse kulephera kugona Usiku onse kulephere kugona ah ah ay Kodi ndi malodza Mwina ndi minyama olo tsoka Kapena mwina ndalumidwa ndi njoka Kapena mwina ndalumidwa ndi njoka ah ah ay Iwe Nabetha tizivutika Iwe utangoshala pamenepo tabwera Kodi Nabetha kapena undithandiza Iwe Nabetha kanda Kanda, apapa Kanda, kanda, (mmh apapa) Kanda, apopo Kanda, pamenepo Kanda, pameneposo Thupi langa kunyelenyetsa mama Palipose kunyelenyetsa mama Thupi langa kunyelenyetsa mama Palipose kunyelenyetsa, ndigofuna ndingo Ndingofuna ndingo Ndingofuna ndingo, (yeah Grin) Uh ha uh ha Kodi ndi chitedze Ndalakwa chani kuti chindikwele Ine ndikulephela kumvetsa Ine ndikulephela kumvetsa uh uh ay Kodi ndi chitedze Ndikusowa myengo oti ndigwire Kumva kuning'ina ngati minga Kumva kundindinga ngati ndingo ah ah ay Iwe Nanyoni Ndidzivutika Utangokhala pamenepo tabwela Poti nabetsa, kapena undithandiza Iwe Nanyoni Kanda, kanda Kanda, kanda (apapa) Kanda, (apopo) Kanda, (ukoko) Kanda, (ichocho) Kanda Thupi langa kunyelenyetsa mama Palipose kunyelenyetsa mama Thupi langa kunyelenyetsa mama Palipose kunyelenyetsa, ndigofuna ndingo Ndingofuna ndingo Ndingofuna ndingo, (I say they call me Orezi) Uh ha uh ha Hey baby you know that your body buh So bring it closer girl don't be shy Wanna do some nasty to you I got the goshen i got the goose Hold me like down low Baby take off your blouse Nobody afi know Keep it on the down low low low, baby eeh eeh eeh eeh Girl i've been waiting for a very long time, ooh ooh ooh ooh Tellin' me come alo de fool me one time I see you girl ade chicco From body then you go legal So lets not waste anytime Girl let's get freaky tonight Thupi langa kunyelenyetsa mama Palipose kunyelenyetsa mama Thupi langa kunyelenyetsa mama Palipose kunyelenyetsa, ndigofuna ndingo Ndingofuna ndingo Ndingofuna ndingo Uh ha uh ha