One, Two (One, Two) Namadingo Alipo, alipo ondi- Alipo, alipo ondi- International Alipo ondidelera M'maso mwawo ndimachepera Akuti nyimbo zanga samvera Ndi-ndi, ndipo sine oyenera kumanditchula dokotala Ndilibe PhD papepala Angondipatsa udokotalawu Nde wina akamva Doc sasangalala Eti mpaka kunditchula kuti wamsala Ndingothokoza Mulungu oyera amandikondera Madalitso akubwera tikulemera Namadingo most followed mumfuse [?] Adzavomeleza too late (Pano iwo ndi lalala) Kuti mwana uja ndi dolo (Pano iwo ndi lalala) Koma too late, too late, too late (Pano iwo ndi lalala) Koma too late, too late, too late (Pano iwo ndi lalala) Rrr-rah, dats de fire dere Mfumu yazinyawu ija Flow so sick I need a doctor to feature I am not an average joe, they pay me what you make in a year for a show In a deck of cards I'm the jokеr I'm the extremе opposite of mediocre Simungamake ndine messi pa soccer Grin ndi messi pa soccer (Yeah) Too many international awards I'm representing Malawi, your bro Doing this till I grow old Nanga timea squire? Ndili pa billboard Ena adzavomeleza too late (Pano iwo ndi lalala) Kuti mwana uja ndi dolo (Pano iwo ndi lalala) Koma too late, too late, too late (Pano iwo ndi lalala) Koma too late, too late, too late (Pano iwo ndi lalala) Ena adzavomeleza too late (Pano iwo ndi lalala) Kuti mwana uja ndi dolo (Pano iwo ndi lalala) Koma too late, too late, too late (Pano iwo ndi lalala) Koma too late, too late, too late (Pano iwo ndi lalala) Muliponso ena all over the world Mumadeleledwa kuchepetsedwa If you visualize it, you're bound to do it Life's a jungle, me I rumble through it If I can do it, y'all can do it From the frontline, put your back into it Ena adzavomeleza too late (Pano iwo ndi lalala) Kuti mwana uja ndi dolo (Pano iwo ndi lalala) Koma too late, too late, too late (Pano iwo ndi lalala) Koma too late, too late, too late (Pano iwo ndi lalala) Ena adzavomeleza too late (Pano iwo ndi lalala) Kuti mwana uja ndi dolo (Pano iwo ndi lalala) Koma too late, too late, too late (Pano iwo ndi lalala) Koma too late, too late, too late (Pano iwo ndi lalala) Joe Gwaladi aseh uli bho?