Kishore Kumar Hits

Gwamba - Anabwela Yesu şarkı sözleri

Sanatçı: Gwamba

albüm: Jesus Is My Boss


Awo anali abusa
Anthu ankawanyadila
Pomwe iwo amadutsa
Anthu ankawagwadila
Koma zachisoni tsiku lobwera Yesu litafika
Tsoka aja tinkati ndioyela aja sadzapita
Mayina opita kumwamba
Dzina lawo linabisika
Ochimwafe titani nanga?
Mudzi onse kubalalika
Mmm! zachisoni kuwona
Kuona a Christu akulowa
Abusa awo akanika
Sometimes tikaona munthu don't judge
Ukaona munthu keep quiet
Poti sumaziwa mumtima muli chani
Sometimes ukaona munthu don't judge
Ukaona munthu keep quite
Poti sumadziwa mumtima muli chani
Anabwera Yesu kudzatenga ake
Onse woyera mtima
Anabwera Yesu kudzatenga ake
Onse owomboledwa
Anabwera Yesu kudzatenga ake
Onse woyela mtima
Anabwera Yesu
Ndipo ndinamuona ine ndimaso anga yeah
Pa tsiku lachiweruzo ndinkawona ngati ndizalowa kumwamba
Poti ndimayimba zauzimu
Kusisimutsa anthu m'midzimu (yeah)
Koma ine ndinadabwa
Ambuye kundiona ine sakulabada (hee)
Mpaka ine ndinagwada
Nkumalila ndili pansi ndili cha gada (yeah)
Mayina opita kumwamba
Dzina lawo linabisika
Ochimwafe titani nanga?
Mudzi onse kubalalika
Lapa lapa lapa poti pano nthawi yatha kale
Lapa lapa lapa bwezi kumwamba ndi talowa m'bale
Sometimes umaona munthu dont judge
Ukaona munthu keep quiet
Poti siumaziwa mumtima muli chani
Sometimes timaona munthu don't judge
Ukaona munthu keep quiet
Poti sumaziwa mumtima muli chani
Anabwera Yesu kudzatenga ake
Onse woyera mtima
Anabwera Yesu kudzatenga ake
Onse owomboledwa
Anabwera Yesu kudzatenga ake
Onse woyela mtima
Anabwera Yesu
Ndipo ndinamuona ine ndimaso anga yeah

Поcмотреть все песни артиста

Sanatçının diğer albümleri

Benzer Sanatçılar