Kishore Kumar Hits

Gwamba - Kusasa Mawu şarkı sözleri

Sanatçı: Gwamba

albüm: Kusasa Mawu


Major one records
Ndiyimbila Yehova ine
Mpaka kusasa mawu ine
Wandipatsa ka girl timaso ta ngero
Lero ndisasa mawu ine
Ndiyimbila Yehova yo
Mpaka kusasa mawu ine heh eh
Wandipatsa ka girl timaso ta ngero
Lelo ndisasa mawu
Yeah Ambuye mwadyetsa mbalame zosalima
Kutionetsa njira nditangoima
Kufewetsa moyo wanga ukulimba
Mwandipatsa mkazi mkona ndikuyimba
Yeah nditangomuona basi
Thupi langa lose kugwidwa dzanzi
Kudzigudubuza gudubuza pansi
Amama ine ndapeza mkazi
Lero ndineneletu
Ndithokoze kwa Yesu
Zobisala ayi
Za mitala ayi
Lero wanga ndamupeza
Ama ma ma ma ma, (ah yeah)
Major one akudalitsa, (ah yeah)
Lero m'mbuyo pang'ono
Ndipo manong'onong'o
Ndipo lero simtaya nthawi
Ndiyimbira Yehova ine
Mpaka kusasa mawu ine
Wandipatsa ka girl timaso ta ngero
Lero ndisasa mawu ine
Ndiyimbila Yehova yo
Mpaka kusasa mawu ine heh eh
Wandipatsa ka girl timaso ta ngero
Lelo ndisasa mawu
Yo, kakabwera ngati kasavaye
Nde kakuti kabwelaso mawa, (shaa)
Zokongola zokhazo zitaye
Nthawi zonse ngati kakuchoka shower
Olo mu short hair kasadaye
Mawonekedwe samakathawa
Zachibwanazi pa easy kaye
Na uyu yekha ndukumara
Lero ndineneletu
Ndithokoze kwa Yesu
Zobisala ayi
Za mitala ayi
Lero wanga ndamupeza
Ama ma ma ma ma, (ah yeah)
Major one akudalitsa, (ah yeah)
Olo m'mbuyo pang'ono, ayi
Umva manong'onong'o, ayi
Ndipo lero simtaya nthawi
Ndiyimbira Yehova ine, (ndiyimbira Yehova ine)
Mpaka kusasa mawu ine, (mpaka kusasa mawu ine)
Wandipatsa ka girl timaso ta ngero
Lero ndisasa mawu ine
Ndiyimbila Yehova yo
Mpaka kusasa mawu ine heh eh
Wandipatsa ka girl timaso ta ngero
Lelo ndisasa mawu
Ndiyimbira Yehova
Mpaka kusasa mawu ine
Wandipatsa ka girl timaso ta ngero
Lero ndisasa mawu ine
Ndiyimbila Yehova yo
Mpaka kusasa mawu ine heh eh
Wandipatsa ka girl timaso ta ngero
Lelo ndisasa mawu

Поcмотреть все песни артиста

Sanatçının diğer albümleri

Benzer Sanatçılar