Kishore Kumar Hits

Gwamba - Sindichoka şarkı sözleri

Sanatçı: Gwamba

albüm: Mama Said God First


Zambiri yanu ndinamva
Akhungu onse osamva
Ena wosayenda
Kungowakhuza Inu nyengo zawo zinasitha
Nane ndifuna mundikhudze
Chonde Musandipitilire
Ndatsegula manja (mulore zimu wanu mwa ine ukhazikike)
Yesu anamva mphamvu zikuchoka
Nzimayi winawake atamugwira
Mavuto ake onse ndikuchoka
Amadwala basi iye ndikuchira
Nane Mbuye wanga Mundigunde
Mukandiwolotse pa mafunde
Ndikudziwa pena ndine khutukumve
Koma mukafuna kukandi user mundiyuze
Mukandikhudza, nyengo zanga zisitha
Mukandikhuza nyengo zanga
Mumachita zazikulu izo ndinamva
Simkaika konse
I wanna see your glory
I wanna testify ukulu wanu ndiwuone
Koma sindichokachokachoka
Mpaka Mundikhudzekhudzekhudze
Koma Sindichokachokachoka
Mpaka mundikhudze khudze ine
Mbuye wanga chonde mundikhudze
Ndikalakwitsa chonde mundiuze
Ndikamachepa chonde mundikuze
Osalora Satana andizunze
Zolakwika zonse muzichotse
Inu ndi amene mungakonze
Pandekhapa palibe ndingachite
Nde chonde mudzindisamalira nthawi zonse
Chonde musalore moyo wanga
Satana adzaleponso sizanga
Chonde musalore Mbuye wanga
Satana akolope moyo mwanga
Mukandikhudza, nyengo zanga zisitha
Mukandikhudza nyengo zanga
Mumachita zazikulu izo ndinamva
Simkaika konse
I wanna see your glory
I wanna testify ukulu wanu ndiwuone
Koma Sindichokachokachoka
Mpaka mundikhudzekhudzekhudze
Koma sindichokachokachoka
Mpaka mundikhudze khudze ine
Mpaka mundikhuze ine yeah aaw aah
Mpaka mundikhuze iye yeah aaw aah
Mukandikhudza, nyengo zanga zisitha
Mukandikhudza nyengo zanga
Mumachita zazikulu izo ndinamva
Simkaika konse
I wanna see your glory
I wanna testify ukulu wanu ndiwuone
Koma Sindichokachokachoka
Mpaka mundikhudzekhudzekhudze
Koma sindichokachokachoka
Mpaka mundikhudze khudze ine
Mumachita zazikulu izo ndinamva
Simkaika konse
I wanna see your glory
I wanna testify ukulu wanu ndiwuone
Koma Sindichokachokachoka
Mpaka mundikhudzekhudzekhudze
Koma sindichokachokachoka
Mpaka mundikhudze khudze ine

Поcмотреть все песни артиста

Sanatçının diğer albümleri

Benzer Sanatçılar