Kishore Kumar Hits

Gwamba - Akondakitale şarkı sözleri

Sanatçı: Gwamba

albüm: Mama Said God First

Yi, aye-iye-yah
Aye-iye-yah
Akondakitale ndalama ndalipirayi ndati ndipemphe, mundibwenzereko chenje

Ulendo wanga ukathera ku Lilongwe, m'deport
Koma ndipemphe, mundibwenzereko chenje
Inu ulendo wanga ukathera ku Lilongwe, m'deport
Koma ndipemphe, mundibwenzereko chenje, yi
Aish, ndalama nde yavuta pa Nyasa
Daily fans kumayisaka
Sikuwona zoti ndiwe shasha
Kumenya business basi kumayitsatsa
Nde mukapeza ka ndalama Sister, chonde kumakagwiritsitsa
Mukamagona nako kukafunditsa
Kwachuluka mbava nde muzikabisa
Yi, ndikupempha mundithandize
Yi, wangondivuta ndi uphawi (ayi)
Ah, ah
Akondakitale ndalama ndalipirayi ndati ndipemphe, mundibwenzereko chenje
Inu akondakitale ndalama ndalipirayi ndati ndipemphe, mundibwenzereko chenje
Ulendo wanga ukathera ku Lilongwe, m'deport
Koma ndipemphe, mundibwenzereko chenje
Inu ulendo wanga ukathera ku Lilongwe, m'deport
Koma ndipemphe, mundibwenzereko chenje, yi
Aish, conductor pokwera umati 100 ndangokhala pansi ukuti 120
Aseh, osaziyamba zinazi
Muno sindichoka ngati sundipatsa chenje
Wekha ukudziwa dollar ili pa minga
Povaya kudedza pena kukwera njinga
Nde ngati umayesa ngati ukundiyimba
Lero lonkha wandilira sindiyimva
Yi, ndikupempha mundithandize
Yi, wangondivuta ndi uphawi (ayi)
Ah, ah
Akondakitale ndalama ndalipirayi ndati ndipemphe, mundibwenzereko chenje
Akondakitale ndalama ndalipirayi ndati ndipemphe, mundibwenzereko chenje
Ulendo wanga ukathera ku Lilongwe, m'deport
Koma ndipemphe, mundibwenzereko chenje
Ulendo wanga ukathera ku Lilongwe, m'deport
Koma ndipemphe, mundibwenzereko chenje, yi
Aish, komanso Yesu akufuna change mama
Koma change akufuna iye si ndalama
Akufunitsitsa inuyo makamaka mutasintha ndikuyamba kumutsata
Mapemphero ndi hustle ya uzimu
Mukapusa tsiku lomaliza, no change
Mapemphero ndi hustle ya uzimu
Ukapusa tsiku lomaliza, no change
Yi, ndikupempha mundithandize
Yi, wangondivuta ndi umphawi (ayi)
Ah, ah
Akondakitale ndalama ndalipirayi ndati ndipemphe, mundibwenzereko chenje
Akondakitale ndalama ndalipirayi ndati ndipemphe, mundibwenzereko chenje
Ulendo wanga ukathera ku Lilongwe, m'deport
Koma ndipemphe, mundibwenzereko change
Ulendo wanga ukathera ku Lilongwe, m'deport
Koma ndipemphe, mundibwenzereko chenje, yi

Поcмотреть все песни артиста

Sanatçının diğer albümleri

Benzer Sanatçılar