Kishore Kumar Hits

Gwamba - Ngati Inu şarkı sözleri

Sanatçı: Gwamba

albüm: True Independence


Yo
Ndika khala ndekha ndekha
Ndazimitsa phone
Ndangoshala penapake ndili lonely
M'mutu mwangamu mumayenda zambiri
Reflection yeni yeni yomwe ine ndili
Koma ndikakhala fanzi ikuona
Ndimafuna ndidzinama ngati obona
Komano kweni kweni m'manamiza ndani?
Beef thupi ndi nzimu wanga udane
Ndikakhala mu church ndimamenya malilime
Komano nzimu oyera sumakhkala uli ndi ine
Pakamwa pakuthoka koma m'mutu muli zina
Wolungama pamaso koma mkatimu ndi sinner
Ngakhale mchipinda
Mopanda amene akuona
Ulengeni mtima wangawu yeah
Ukhale ngati inu! ooh!
In everything i do! ooh!
Nkhale ngati inu! ooh!, (mfanane nanu Baba)
In everything i do! ooh!, (mfanane nanu Baba)
Nde in everything i do
Mundithandize kukhala wodekha
Poti ndinabadwa ndipo ndidzapita ndekha
And it's true ndi zapadzikozi ndimakopeka
Tsoka mukafuna kunditenga osakonzeka
Pena ndimaseka mumtima muli misozi
Anthu amangowona mkamasekelera chonchi
Koma za mu mtima mwanga amadziwa ndi m'modzi
Nde pakati pa dziko ndi Yesu ndisankhe m'modzi
Pena ndimaseka mumtima muli misozi
Anthu amangowona mkamasekelera chonchi
Koma za mu mtima mwanga amadziwa ndi m'modzi
Nde pakati pa dziko ndi Yesu ndisankhe m'modzi
Ngakhale mchipinda
Mopanda amene akuona
Ulengeni mtima wangawu yeah
Ukhale ngati inu! ooh!
In everything i do! ooh!
Nkhale ngati inu! ooh!, (mfanane nanu Baba, mfanane nanu Baba)
In everything i do! ooh!, (mfanane nanu Baba, mfanane nanu Baba)
Pakamwa panga mupakonze
Mtima wangawu muwupinde
Nzeru zangazi muzipinde
Zochita zanaga ziyamike inu
Munandilenga bwinobwino
Kufuntha kwanga kwawonjeza
Ndizipemphelera chakudya
Olo anzanga asakuwona
Munandilenga kwa ndekha
Munandipatsa za ndekha
Ooh! ooh! ooh!
Ngakhale mchipinda, (ooh!)
Mopanda amene akuona, (alone)
Ulengeni mtima wangawu yeah
Ukhale ngati inu! ooh!
In everything i do! ooh!
Nkhale ngati inu! ooh!, (mfanane nanu Baba, mfanane nanu Baba)
In everything i do! ooh!, (mfanane nanu Baba, mfanane nanu Baba)

Поcмотреть все песни артиста

Sanatçının diğer albümleri

Benzer Sanatçılar