Kishore Kumar Hits

Gwamba - My Daily Worship şarkı sözleri

Sanatçı: Gwamba

albüm: True Independence


I have never seen, no one like you (no one like you)
No one like you (no one like you)
Yesu (Yesu)
I have never seen, no one like you (no one like you)
No one like you (no one like you)
Yesu (Yesu)
Ambuye (Ambuye)
Ambuye (Ambuye)
Ndikuthokoza Ambuye (Ndikuthokoza Ambuye)
Ambuye (Ambuye)
Ambuye (Ambuye), Ndikuthokoza Ambuye
Eeh eh eh
Iyi ndi nyimbo yafuko langa, my daily worship
Ndikuvutika simunandisiye chonchi
Kundionesa ufumu wanu kundipasa chi plot
Nde kulikose ndingapiteko tili limodzi
Abale ndi alongo zikavuta amathawa
Mavuto, pa mtendele simumansintha ma colour
Nde zingavute bwanji ndimayesesa ndisadande
Poti masiku sakoma onse, ndi nthawi chabe
Iyi ndi daily worship, nyimbo yafuko langa
Kenako ukamvera uzipezamo ka bata
Osamathamangila kunena kuti sanayankhe
Chifukwa olo mpweya tikupumau ndi wake
Pali chinthu chimodzi chomwe mumalakwisa brazi
Mufuna mudwale kaye kuti muyamikire nthanzi
Wina amwalire kuti muyamikire moyo
Akachedwa kuyankha mumasiya kukhala loyal
Ndeno Tate wanga ndufuna kukhala munthu wa humble
Poti ndikuziwa mumapasa, mumalanda
Komanso ndukufuna ndikhale chitsanzo
Mfana wa mature poti chibwana chimalanda
Kuchepesa anga, bible likhale mzanga
Munthu kundiyamba ine kukhululuka nsanga
Kupewa ma blanda, Jajah mu mtima mwanga
Tsiku lomalidza kuchongetsa dzina langa
Ambuye (yea yea yea yea)
Ambuye (yea yea yea yea)
Ndikuthokoza Ambuye (Ndikuthokoza Ambuye)
Ambuye (yea yea yea yea)
Ambuye (yea yea yea yea)
Ndikuthokoza Ambuye (Ambuye eeh)
Uuh uh uuh
I have never seen, no one like you (no one like you)
No one like you (no one like you)
Yesu (Yesu)
I have never seen, no one like you (no one like you)
No one like you (no one like you)
Yesu (Yesu)
Ambuye
Ambuye (no one like you)
Ndikuthokoza Ambuye (Yesu)
Ambuye
Ambuye (no one like you)
Ndikuthokoza Ambuye (Yesu)
Uuh yeah yeah
Uuh yeah yeah

Поcмотреть все песни артиста

Sanatçının diğer albümleri

Benzer Sanatçılar