Kishore Kumar Hits

Mfumu Hyphen - Tsidya Lina şarkı sözleri

Sanatçı: Mfumu Hyphen

albüm: Tsidya Lina


Yo yo yo
(Tricky beats ooh ooh)
Mmh mmh
Mmh mmh, (yeah)
Look eh, tawoloka uone
Zomwe amaona akatseka maso nzomwe zili kuseli kwa dzikope
Wekha ungamaope, utadziwa zomwe amabisa
Zomwe samawonetsera pa nkhope
Umangowona nkhonde
Atazijudula kusiya mulomo palipose phazi litaponda
Now i'd rather be lonely
In Jah de creater we stand when i fall ngakhale ena atizonde
Ena atikonde
Ena atinyoze, kupondelezana ndi kosayamba usagonje
Sometimes water is thicker than your blood
How they really feel is what they will be saying behind your back
Uwu ndi ufulu wa nkhondo
Zotikamba nde siziwathela, the evil munthudi ndi chilombo
Ukudutsa muzikhomo, dalira Namalenga
Udzaona ukulu wake ukapinda bondo
Mtima wa nzako ndi tsidya lina
Usamenye mpira bwinodikira ndabinya
Usamapusitsike nza pa social media
Anthu ena amakupopa atayika tsinya
Mtima wa nzako ndi tsidya lina
Ati ndiwe hule poti umakonda kuvina
Mtima wa nzako ndi tsidya lina
Kukupopa koma kuseli manena zina
Yah eh, angopumira m'mwamba
Ularo wotilumikiza nawo tinawotcha komabe amatikamba
Awawa anali anzanga
Koma tinatayana, amatengerapo danga pawunsamaliya wanga
Dzuka Malawi wanga
Ndiwavetsetsa poti pasambira fulu kapolo afuna kusamba
Afuna kulanda, but me on my music that's God's union
No man can put a slunder
Zifwamba za mtendere wamu mtima
Nsangala kupha loto la munthu wina
Umadziwa ndiye zikawathina
Amandikumbukira kuchokera tsidya lina
Fulu wa fuko, those misdeeds will come back to you
Don't get caught in a loop
Caught in this world of things that's only fools goal
They can't speak on the things that only you know
Mtima wa nzako ndi tsidya lina
Usamenye mpira bwino dikira ndabinya
Usamapusitsike nza pa social media
Anthu ena amakupopa atayika tsinya
Mtima wa nzako ndi tsidya lina
Ati ndiwe hule poti umakonda kuvina
Mtima wa nzako ndi tsidya lina
Kukupopa koma kuseli manena zina
Anthu ena behaviours' stinker than sewage
Amadikira upale then akuwe i knew it
Amatsogoza kujaja kunena sumatha
As if nginiyo iwowa can do it
To kill you oh yes your best friend is able
Samala ndiyemwe chilichonse amati big up, cheers
Atakuloza mfuti under table
Munthu samafuna level yake ufikepo
Mtima wa nzako ndi tsidya lina
Usamenye mpira bwino dikira ndabinya
Usamapusitsike nza pa social media
Anthu ena amakupopa atayika tsinya
Mtima wa nzako ndi tsidya lina
Ati ndiwe hule poti umakonda kuvina
Mtima wa nzako ndi tsidya lina
Kukupopa koma kuseli manena zina

Поcмотреть все песни артиста

Sanatçının diğer albümleri

Benzer Sanatçılar