Kishore Kumar Hits

Phyzix - Wife Material - Amapiano Version şarkı sözleri

Sanatçı: Phyzix

albüm: Wife Material (Amapiano Version)


Sonye Entertainment
Kukakhala kunjaku kwacha boo
Malawi Music dot com
Nyimbo za chimalawi
Kukhala kunjaku kwacha boo
Ndachita kudzadzamo momomo
Wife material tiliyo tiliyo
Wife mati ti ti ti
Ndinapeza babie anthu adziwe
Sindimachibisa sichapadziwe
Yemwe zikumuwawa adiwe
Komatu ichichi ndi changa chi Lindiwe
Sichingadzakupatse patse phindi iwe
Chimakhala chili ndi Ine
Udzimva iwe
Vuto lake iweyo kudzimva iwe
Umangogwira akazi openga ma by zweee
Zaife ndi zokoma zothira kale
Sitimvesana kuwawa tsabola wakale
Uyuyu ndi wanga si tempory
Ndikanena kuti ndi mugaya si phale
Kutetha ngati nali samalani abale
Akugungira sugar onyambisisa mbale
Mkazi you ngoiwalisa abale
Amakomedwesa ngati andale
(Very good very good)
Mamie ndinu chimkazi chowoneka boo
Mumachita kukhala ngat a video
Mamie muli pure ngat ka viligo
Mukadzafuna banja ife tilipo
Ndinu wife material tiliyo tiliyo tiliyo
Wife mati ti ti titi
Wife material tiliyo tiliyo tiliyo
Wife thi thi thithi
(Yeee)
Ichi ndi chindiwo koma si mpiru
Sindinachite kuchiba koma ndi chi deal
Ichi ndi chibabe chodzadza fill
Dzina lake ndinaliyika kale pa will
Chimandikumbusa Mag Maupili
Mahope anga aku Primary Ku mphungu
Tili mafana oyakhula chizungu
She had a chocolate skin ndimamufila khungu
Chibabe changachi chanfipatsa khungu
Ndikayenda ntaunimu sindiona buthu
Ndadwala chikondi 10 pa 10
Chachita kundifika pempeni
Ndaonera man ndimalizeni
Sindipepha ambuye ndi chilitseni
Izizi sizagulu siza mmemo
Ineyo ndili mmomo mmenemomo
Very good very good
Mamie ndinu chimkazi chowoneka boo
Mumachita kukhala ngat a video
Mamie muli pure ngat ka viligo
Mukadzafuna banja ife tilipo
Ndinu wife material tiliyo tiliyo tiliyo
Wife mati ti ti titi
Wife material tiliyo tiliyo tiliyo
Wife thi thi thithi
Girl you the wife material
I just want make you my wife ooo
Girl you the one in a million ooo
This feeling for you I can't deny ooo
Iwe ndiwe mkazi oneka boo
Ooneka boo oooneka boo
Iwe ndiwe chimkazi chooneka boo
Chooneka boo chooneka boo
Iwe ndiwe mkazi wofitha boo
Wofitha boo wofitha boo
Iwe ndi chimkazi chofitja boo
Chofitha boo chofitha boo
Mamie ndinu chimkazi chowoneka boo
Mumachita kukhala ngat a video
Mamie muli pure ngat ka viligo
Mukadzafuna banja ife tilipo
Ndinu wife material tiliyo tiliyo tiliyo
Wife mati ti ti titi
Wife material tiliyo tiliyo tiliyo
Wife thi thi thithi
Aaaayaaa
Ati Kolokoto
Mutu wanga zwee
Kolokoto
Very good very good
Very good very good

Поcмотреть все песни артиста

Sanatçının diğer albümleri

Benzer Sanatçılar