Kishore Kumar Hits

Eli Njuchi - Zitatu şarkı sözleri

Sanatçı: Eli Njuchi

albüm: The Book of Z


Mmh mmh
Mmh mmh
Ndinayesako, ndinayesako
Zokondanazi ndinayesako (aaah)
Ndalora aah chifuniro ndalora aah
Mmh, ay, tiyambe?
I still remember mene ndinkamvera
Tears of joy ndinkafuna kulira
Anadzandiyang'ana nkudzandimwetulira
She was like, "Mmh man mumalimbikira"
Dzaka zitatu, ndinagubira zaka zitatu
Ndisakudziwa hustle zaka zitatu
Ndisali Eli Njuchi zitatu (Njuchi zita)
Zilibe kanthu bola asadziwe anthu
Zikhoza kundivuta kwathu
Sungalimvetse Banja lathu (banja la)
Chaka chomwecho ndinayamba kulowa studio
After some months tayamba Kumveka radio
After some months tajambula ka video
Kwinaku tidumphe tifike form four
Zinthu zinayamba kuphweka
Ndinayamba kumva nkhani ati ndatchuka
Azinzanga nawo anachuluka
Ndinayamba kusintha zochita
3:00 am ndinalandila call
A Eli Njuchi I hope muli bho
I realized something was wrong
Cause always ankanditcha Chifuniro
Zaka zitatu tili limodzi zaka zitatu
Unkandikonda zaka zitatu
Nde sudzandiona kwa dzaka zitatu (dzaka zita!)
The call ended
Mawa lake ndinanyamuka
Ndinafika kwawo, Ukufuna ndani?
Annie kuno anasamuka
That's when I realized zibwana zanga, zolakwa zanga
Pepani sindikamba zibwana zanga, zolakwa zanga (Mmmh)
Chaka chimodzi chinapita
Eli Njuchi anamveka
Bus pa Zebra ndinatsika
Nsewu wakudeni ndinalunjika
And then I saw a pretty lady coming my way
Titayandikana anali Annie
Anayamba kugwetsa msozi ukutita hagana
And then she told me soon
Akhala ndi mwana

Поcмотреть все песни артиста

Sanatçının diğer albümleri

Benzer Sanatçılar