Kishore Kumar Hits

Eli Njuchi - Zilu şarkı sözleri

Sanatçı: Eli Njuchi

albüm: The Book of Z


Yeah yeah
Yeah yeah
Mesa mumkandikonda
Mesa mumkandikonda
Nanga bwanji lero mwasintha
Bwanji lero mwasintha
Mesa mumkandikonda
Mesa mumkandikonda
Bwanji lero mwasitha
Bwanji lero mwasintha
I'm fine, zonse zilibwino
Izi ndi zomwe ndimawayankha
Anzanga komaso alendo
Mmh bola moyo
Oh bola moyo
Ngati ndikupuma ndichisomo
Chotsani manja zonse zilibwino
Ndinasanduka kapolo nyumba mwanumo
Kaya gawo langa liti m'moyo mwanumo
Zokoma zonse zinatha khomo lanulo
Ndalimba mtima lero lokha mundiuze
Mesa mumkandikonda
Mesa mumkandikonda
Nanga bwanji lero mwasintha, (chilungamo)
Bwanji lero mwasintha, (chilungamo)
Mesa mumkandikonda
Mesa mumkandikonda
Nanga bwanji lero mwasintha, (chilungamo)
Bwanji lero mwasintha, (chilungamo)
Mesa mumkati ndine golide
Mesa mumkati ndine ka ngelo
Atsika mtengo liti ma Chiyembe
Kuti muwazule mapiko
Ndinali pompa musanapeze zonsezi
I was the one to tell you dzuka ukamagona
Ndimkasekedwa ndi anzanga ali m'ma benz
Ndimkanyozedwa ndi makolo akamva za iwe
Pano mwakula ndinthu zayamba kuyenda
Mwayamba kutchulidwa njonda
Misozi ndikamakumbuka sizoona
Ndachotsa mantha lero lokha mundiuze
Mesa mumkandikonda
Mesa mumkandikonda
Nanga bwanji lero mwasintha, (chilungamo)
Bwanji lero mwasintha, (chilungamo)
Mesa mumkandikonda
Mesa mumkandikonda
Nanga bwanji lero mwasintha, (chilungamo)
Bwanji lero mwasintha, (chilungamo)
Kodi manebawa adzivela ife
Kundimenyaku mukufuna ndife?
Anawa tiwalera bwanji ife, ooh
Kodi manebawa adzivela ife, ooh
Anawa tiwalera bwanji ife, mmh yey
Mesa mumkandikonda
Mesa mumkandikonda
Nanga bwanji lero mwasintha, (chilungamo)
Bwanji lero mwasintha, (chilungamo)
Mesa mumkandikonda
Mesa mumkandikonda
Nanga bwanji lero mwasintha, (chilungamo)
Bwanji lero mwasintha, (chilungamo)
Mesa mumkandikonda
Mesa mumkandikonda
Nanga bwanji lero mwasintha, (chilungamo)
Bwanji lero mwasintha, (chilungamo)
Mesa mumkandikonda
Mesa mumkandikonda
Nanga bwanji lero mwasintha, (chilungamo)
Bwanji lero mwasintha, (chilungamo)
Njuchi, njuchi

Поcмотреть все песни артиста

Sanatçının diğer albümleri

Benzer Sanatçılar