Kishore Kumar Hits

Eli Njuchi - Kumpanje şarkı sözleri

Sanatçı: Eli Njuchi

albüm: The Book of Eli


Ay yeah! lelele
Ay yeah! lelele
Njuchi
Kusowa poyambila
Mose munachokera
Olo ka ndede kutulukila
Tidziti ndalamazo mukungomwela
Kuno mbumba zagwira nsewu
Mwana wanu Saulos analidziwa khasu
Mtundu uliwonse wa mbewu
Kumufuna Jane pompo mulandira yankho
Mbuye, chonde bwelaniko
Ngati zikuvuta mudzayese kuno
Mayi Malawi!
Kwanu mkwanu
Kumpanje, kunkuno
Kumpanje
Ngati nkhani ili ya golide (golide)
Moyo ndi wodula kuposa golide (golide)
Kwanu mkwanu
Kumpanje, kunkuno
Kumpanje
Ngati nkhani ili ya golide (golide)
Moyo ndi wodula kuposa golide (golide)
Mbuye, chonde bweraniko
Ngati zikuvuta mudzayese kuno
Mayi Malawi!
Kwanu mkwanu
Kumpanje, kunkuno
Kumpanje
Ngati nkhani ili ya golide (golide)
Moyo ndi wodula kuposa golide (golide)
Oh ine mantha
Ndikamva za xenophobia
Angozo chonde bweraniko
Mudzafele zina izi nza padziko
Kulibwino kugona mu mdima
Osati kugona ndi manja mu mtima
Palibe vuto olo munasochela
Kaya ndi uchidakwa tidzawulandila ah
Mbewa ya manyazi inafela ku una
Ndamva zoti mulibe ngakhale pogona
Kwanu kuno mkwa mavuto ndi zo-ona
Koma pomwe mwafikapo zanyanya
(Siwanu samachita bwino)
Ena amakangochulukitsapo mavuto
Kungoti a uje ali komweko basi nanuso mukayeseko
Mukathela komweko
Kwanu mkwanu
Kumpanje, kunkuno
Kumpanje
Ngati nkhani ili ya golide (golide)
Moyo ndi wodula kuposa golide (golide)
Kwanu mkwanu
Kumpanje, kunkuno
Kumpanje
Ngati nkhani ili ya golide (golide)
Moyo ndi wodula kuposa golide (golide)
Wa weh Kumpanje
Wa weh Kumpanje
Wa weh Kumpanje
Wa weh Kumpanje
Kwanu mkwanu Kumpanje
Konkuno Kumpanje
Kwanu mkwanu Kumpanje
Konkuno Kumpanje
Ah ah Eli oh
I don't just love Malawi
I also love my beautiful people

Поcмотреть все песни артиста

Sanatçının diğer albümleri

Benzer Sanatçılar