Mmm
Naomi dzuka kwacha (Naomi dzuka kwacha)
Nthawi silinawe (nthawi silinawe)
Kutola nkhobwe ndi m'mawa (kutola nkhobwe ndim'mawa)
Leronso ungachedwe (leronso ungachedwe)
Amadzuka mwamphamvu (amadzuka mwamphamvu)
Kungozipuputa nkhope (kungozipuputa nkhope)
Amayi lero ndachedwa
Ntchito ndigwira nkabwera
Ndimangire kunsewu (ndithamangire kumsewu)
M'mawa kuli mphepo (m'mawa kuli mphepo)
Amathamanga mwamachawi (amathamanga mwamachawi)
Ndikadzera kwa Lutepo
Ndikampeza sanadzuke
Ndisogole akandipeza (nditsogole akandipeza)
Akaugwira nsewu (akaugwira nsewu)
Amakumana ndi azinzake (amakumana ndi azinzake)
Inde nsewu ndi umodzi (nsewu ndi umodzi)
Otenga anthu kusukulu ndiku msika aah (ndikumsika aah)
Akawaona amasirira
Ali m'ma uniform, ali pamodzi!
M'manja mwawo muli makope (mwawo muli makope)
Iye mwake muli dengu (iye mwake muli dengu)
Kutha mtunda (kutha mtunda)
Thupi litalemedwa (litalemedwa)
Abale lero ndachedwa aah (abale lero ndachedwa aah)
Naomi yenda changu (Naomi yenda changu)
Ufulumire (ufulumire)
Changu (changu)
Ufulumire (Ufulumire)
Ufulumire
Wa aaah (wa aah)
Wa aaah (ufulumire)
Wa aaah (wa aaah)
Wa aaah (Ufulumire)
Kumsika akati afike afike afike
Abale dengu munditule munditule munditule
Amayamba kuyala malonda pa mtengo
Naomi kumsika amagulitsa mango
Yekha yekha dzaka khumi ndi zisanu
Inde kuchepa koma amasunga zinsisi yaa ah
Chinsisi choyamba (chinsisi choyamba)
Malonda a mango samayenda (amango samayenda)
Koma chodabwisa (koma chodabwisa)
Kunyumba mangowo samafika (mangowo samafika)
Chinsisi chachiwiri (chinsisi chachiwiri)
Anamphunzitsa ndi Lutepo (anamphunzitsa ndi Lutepo)
Naomi zamangozi tichedwapo (zamangozi tichedwapo)
Kamba kofuna ndalama zachisoni
Naomi yekha anazipezera chinzibambo (anazipezera chinzibambo)
Kutha ntunda (kutha mtunda)
Thupi litalemedwa (thupi litalemedwa)
Izi kugulu zisafike!
Anthu akadziwa ndimulandu (ndimulandu)
Ndiyeno asadziwe (asadziwe)
Mulandu (mulandu)
Asadziwe (asadziwe)
Asadziwe (asadziwe)
Wa aaah (wa aaah)
Wa aaah (asadziwe)
Wa aaah (wa aaah)
Wa aaah (asadziwe)
Поcмотреть все песни артиста
Sanatçının diğer albümleri