Kishore Kumar Hits

Eli Njuchi - Ziloleni şarkı sözleri

Sanatçı: Eli Njuchi

albüm: The Book of Eli


Njuchi
Mam'mawa dzuwa kuli mame
You see me passing by everyday
M'manja muli saka
I know you follow me
Mumandilondola mobisa
Pomwe ndadusa pamakhala mbewu
Mukandifunsa sin'bisa
Ndine mlimi
Kwanga nkufesa
Mbeu yangayi njowala
Ngati nyenyezi
Ndikawawuza nde samandimvesa
Chita manyazi
Ziloleni, ziphukile
Ziloleni, ziphukile
Ndati lolani ziphukile ngati mtengo
Ngati nthambi zibale zipatso
Ziloleni, ziphukile
Ziloleni, ziphukile
Ziloleni, ziphukile
Lolani ziphukile ngati mtengo
Ngati nthambi zibale zipatso
Ziloleni, ziphukile
Ok sispensa
Tiye tiyambilenso
Mam'mawa mpaka kumadzulo
Ntchito ya no malipiro
Still zina zimapondedwa
Zina kudyedwa ndi mbalame
Zochepa zingapo zimasamalidwa
Zimandikhudza ndisaname
Mbewu, zipatso muzaziyang'anire
Ndizamtsogolo zizandisamalire
Ndipo musadabwe ngati ndithilire
Zimela zagwerapo olo mundisesele
Olo musazitipulire
Muzaziwona zikukula
Olo musazitipulire
Muzaziwona, muzaziwona zikukula
Ziloleni, ziphukile
Ziloleni, ziphukile
Ndati lolani ziphukile ngati mtengo
Ngati nthambi zibale zipatso
Ziloleni, ziphukile
Ziloleni, ziphukile, (yeah)
Ziloleni, ziphukile, (ooh)
Lolani ziphukile ngati mtengo
Ngati nthambi zibale zipatso
Ziloleni, ziphukile
Zili ngati mwini nyimbo
Lolani ndifese mbewu yaluso
Musandiweluze kamba ka nsinkhu, (ooh yeah)
Abale fesani mbewu
Ziphukile
Musazibise fesani
Ziphukile

Поcмотреть все песни артиста

Sanatçının diğer albümleri

Benzer Sanatçılar