Kishore Kumar Hits

Eli Njuchi - Tate Wane şarkı sözleri

Sanatçı: Eli Njuchi

albüm: Tate Wane


Ooh yeah
Njuchi, Tate
Mumandidzutsa ndi chitseko
Mumabwera ma m'bandakucha kusanache
Mumalowa ndi chifungo
Mosachedwa phokoso muli ana
Chomwe ndikhumba ine ndi Tate wane
Muli moyo koma ndilibe Tate wane
Chonde musaziyambe Tate wane
M'malo mwawo menyani ine Tate wane
Mundikonde oh Tate wane
Mundikonde oh Tate wane
Mundikonde oh Tate wane
Mundikonde mundikonde Tate wane

Mumawadzutsa ndi chitseko
Mumapezamo chani m'misonzi yawo
Lero mumenyana ndineyo oh
Tate wane, Tate wane mundikonde
No this don't feel like home
This don't feel like home
Dad mangofuna kukontolora
M'kangofika kulongolola
Inu masten wa sapuma
Kumvananso sim'funa
Koma chomwe ndikhumba ine Tate wane
Muli moyo koma ndilibe Tate wane
Chonde musaziyambe Tate wane
M'malo mwawo menyani ine Tate wane (wane)
Mundikonde oh Tate wane
Mundikonde oh Tate wane
Mundikonde oh Tate wane
Mundikonde mundikonde Tate wane
(Chomwe ndikhumba ine ndi Tate wane)
(Muli moyo koma ndilibe Tate wane)

Поcмотреть все песни артиста

Sanatçının diğer albümleri

Benzer Sanatçılar