Kishore Kumar Hits

Eli Njuchi - Dzina şarkı sözleri

Sanatçı: Eli Njuchi

albüm: Red Flag


Dzina
Ndi dzina liti lingadzankhale
Mwina ndima twins
Wina wammuna Wina wamkazi
Julie I've wrote a letter for you
Mwina John, I've wrote a letter for you
My love
Hello my future daughter
How is school?
Ngat umakonda adad give him high five
Hello my future son
Geli ili bwanji?
Ngati ndili pafupi, ubwele undihage
Pakadali pano
Sindidakumane ndi amai ako
One thing I know
She's a loving and a caring lady
Za obvious, I am the funniest father
Za obvious, I am the very best father
Ukamandiona mu future
Dziwa ndine hero
Ngati ukumadya kugona
Son be greatful
2022 mwanawe, its a tough time for your father
Ma pressure ma pressure
Mwana wamamuna ma pressure
Ndikanali vendor, searching for your better life kumibawa
Ndikanali lova, fighting for your better future ku limbe
Ngati ndiike jump gear, fast forward
Pena ngati ndingogiver ndikudina fast forward
What easily comes easily goes my daughter
Petience
Ndili kubwela see you soon my son
Confidence
Dzina
Ndi dzina liti lingazamukhale
Eti sispence?
Dzina
Ndi dzina liti lingadzankhale
Am gonna watch you grow
Until you grow old
Round of applause
On your wedding and gala

Поcмотреть все песни артиста

Sanatçının diğer albümleri

Benzer Sanatçılar