Wasunga tsitsi walimba
Mu dziko loti ali ndi mwayi
Wometa mpara
Kusamala mutu wake
Wasunga tsistsi walimba
Pakuti mfundu zankhaninkhani
Zayala mphasa
Patsinde pa imvi zake
Chipeso chibwela, (ah chibwela)
Chikakalusa, (oh ah iwe ah)
Mvundula madzi
Monga mvundula madzi
Ati nsabwe zibwela, (mayo)
Ziswa mazira, (ah oh oh)
Mvundula madzi
Monga mvundula madzi
Ah chipeso chibwela, (ah chibwela)
Chikakalusa, oh ah iwe ah
Mvundula madzi
Monga mvundula madzi
Ati nsabwe zibwela, (mayo)
Ziswa mazira (wayi weh ah)
Mvundula madzi
Monga mvundura madzi
Mutuwa uli mbuu
Mutuwa utuwa utuwa
Mutuwa uli mbuu
Ndevu udzizimira wekha
Utuwa uli mbuu
Utuwa utuwa utuwa, (ay weh)
Mutuwa uli mbuu, (oh oh)
♪
Walima munda munjira
Alima mbewu nafesa
Koma tsizinantole
Aseka mwachikhakhali
Ngati chipeso m'mutu mwa mfundu
Abwela nakalasura
Kodi mundawu ngwandani?
Yankha mfundula madzi
Chipeso chibwela, (ah chibwela)
Chikakalusa, (oh ah iwe ah)
Mvundula madzi
Monga mvundula madzi
Ati nsabwe zibwela, (mayo)
Ziswa mazira, (ah oh oh)
Mvundula madzi
Monga mvundula madzi
Chipeso chibwela, (ah chibwela)
Chikakalusa, oh ah iwe ah
Mvundula madzi
Monga mvundula madzi
Ati nsabwe zibwela, (mayo)
Ziswa mazira (wayi weh ah)
Mvundula madzi
Monga mvundura madzi
Utuwa uli mbuu
Utuwa utuwa utuwa
Utuwa uli mbuu
Ndevu udzizimira wekha
Utuwa uli mbuu
Utuwa utuwa utuwa, (ay weh)
Utuwa uli mbuu
Поcмотреть все песни артиста
Sanatçının diğer albümleri