Kishore Kumar Hits

Lawi - Therere şarkı sözleri

Sanatçı: Lawi

albüm: Sunset in the Sky


Ankatikonda amayi
Ngakhale chuma analibe
Moyo siwunawawe
Zonse zinalipo
Ankalawila amayi
M'mundamu nyengo yadzinja
Kukapinda nsana
Pozindikila adzakolola
Palibe olo tsiku limodzi
Anatinyanyala moyo utawawa
Ndiwo zikavuta ankalowa patchire
Tinkasangalala ngakhale timadya therere
Palibe olo tsiku limodzi
Anatinyanyala moyo utawawa
Ndiwo zikavuta ankalowa patchire
Tinkasangalala ngakhale timadya
Aaah aaa aaa aaa therere
Tinkagona nyumba imodzi yodzala ndi mtendere
Aaah aaa aaa aaa therere
Ulemelero sindalama koma ntima wa chimwemwe
Aaah aaa aaa aaa therere
Therere relo mama therere mumtondo
Aaah aaa aaa aaa therere
Therere relo mama therere mumtondo
(Mayako akufuna, ati ukadye mpunga wanyama)
Ankatikonda amayi
Ngakhale chuma analibe
Anangokhala ndi ana
Yehova ankadziwa zakutsogolo
Tinkasewela ngati ana
Opanda nkhawa monga za akulu m'moyo
Anatisenzela amayi
Yehova muwadalitse
Palibe olo tsiku limodzi
Anatinyanyala moyo utawawa
Ndiwo zikavuta ankalowa patchire
Tinkasangalala ngakhale timadya therere
Palibe olo tsiku limodzi
Anatinyanyala moyo utawawa
Ndiwo zikavuta ankalowa patchire
Tinkasangalala ngakhale timadya
Aaah aaa aaa aaa therere
Tinkangona nyumba imodzi yodzala ndi mtendere
Aaah aaa aaa aaa therere
Ulemelero sindalama koma ntima wa chimwemwe
Aaah aaa aaa aaa therere
Therere relo mama therere mumtondo
Aaah aaa aaa aaa therere
Therere relo mama therere mumtondo

Поcмотреть все песни артиста

Sanatçının diğer albümleri

Benzer Sanatçılar