Kishore Kumar Hits

Suffix - Amamva şarkı sözleri

Sanatçı: Suffix

albüm: Before I Sleep


Amayo ine
Mwana wanga ine
Eeih aah mhu mhu mhu
Eish koma

Look amuna anga anapita
Ndine single mom
Chuma anandilanda achibale awo
Anandisiyira mwana m'modzi yekha Love
She's only 16 and she's all i have
Kuti aphunzire school abale ndavutika
Business ya makala kuyikapo mtima
Bola masana okha angodyako nsima
Alimbikire school adzandisunge patsogolo mwina
Walimbikira wapita collage ya mankhwala
Mayi ake asamadzavutike akangodwala
Graduation ceremony yake ili pa mawa
Ubwele kunyumba tidzamuthokoze Mulungu wanga
Tili mkati mopemphera
Mvula kugwa mpaka nyumba kutigwela
Kukanika kumpulumutsa mwana madzi amutenga
Nzamatsenga zitheka bwanji Ambuye mukundimvera?
Ndidziwa misonzi yanu ndiyovuta kupuputa ih yeah
Malingana ndi nyengo zomwe inu mudutsa ah hah ah hah
Adziwa, Chauta wa mwamba
Adziwa, kuliraku amamva
Adziwa, mavuto amamva ah yeah eh eh eh
Pain still fresh i'm asking where to smile
Doesn't make sense at all to be alive
Ambuye mwandisiya m'manja mwa adani
If you really care about us where you are
Pain still fresh i'm asking why to smile
Doesn't make sense at all to be alive
Ambuye mwandisiya m'manja mwa adani
If you really care about us God then where you at?
Yeah our faith is now shaking
She got a lot of questions
She fast to be strong on the other hand
Being tempted to either wisdom from a serpent
Mavuto amabweletsa maganizo oyipa
Umayamba kuganiza anakakhala mwana wanzako
Mavuto amabweletsa maganizoa awiri
Kuyiwala Mulungu kapena kusendera kufupinaye
I pray that God comforts you
I'ts hard to believe that romans 8 it's so true sometimes
I might just so leave it test
To God make sense even when it doesn't make sense
Ndidziwa misonzi yanu ndiyovuta kupuputa ih yeah
Malingana ndi nyengo zomwe inu mudutsa ah hah ah hah
Adziwa, Chauta wa mwamba
Adziwa, kuliraku amamva
Adziwa, mavuto amamva ah yeah eh eh eh

Поcмотреть все песни артиста

Sanatçının diğer albümleri

Benzer Sanatçılar