Kishore Kumar Hits

Beracah - Chifupi Nanu şarkı sözleri

Sanatçı: Beracah

albüm: Inside Out Unplugged


Oh andifinya
Oh anditola
Oh andizunza
It's too much I cannot bear
Moyo opanda inu Baba
Got me living so exposed
Ndaziputila nkhondo
Ndimaona ngati nditha kukhala ndekha ine
But now, now
Mtima Wanga n'nausiya panja
Zoipa ndizodetsa zinaza
Ndizoopsa kukhala opanda inu m'moyo mwanga, mwanga
Pre-chorus
I know He
Safuna kundiona ndikulira ine
I know iye
Afuna kutenga zondiphinja ine
Ndifuna kukhala chifupi Nanu
Kukhala chifupi Nanu
Kukhala chifupi Nanu
Kukhala chifupi Nanu
Mmh mmh mmh
Mmh mmh mmh
Mmh mmh mmh
Mmh mmh mhh
Mmh mmh mmh
Mhh mmh mmh
Yeah, fupi Nanu
Ndakula into something great
Ignored the signs I
Ndazipusisa
That I can have it both ways
You can't have it both ways
To my surprise He still pursues me
With my wavering heart
He remains the faithful
Pouring out his mercy
Mercy
Mtima Wanga n'nausiya panja
Zoipa ndizodetsa zinaza
Ndizoopsa kukhala opanda inu m'moyo mwanga, mwanga
Pre-chorus
I know He
Safuna kundiona ndikulira ine
I know iye
Afuna kutenga zondiphinja ine
Ndifuna kukhala chifupi Nanu
Kukhala chifupi Nanu
Kukhala chifupi Nanu
Kukhala chifupi Nanu
Mmh mmh mmh
Mmh mmh mmh
Mmh mmh mmh
Mmh mmh mhh
Mmh mmh mmh
Mhh mmh mmh
Yeah, fupi Nanu
And I know He
Safuna kundiona ndikulira ine
And I know He
Afuna kutenga zondiphinja ine
Mmh mmh mmh
Mmh mmh mmh
Mmh mmh mmh
Mmh mmh mhh
Mmh mmh mmh
Mhh mmh mmh
Yeah
Ndifuna kukhala chifupi Nanu
Kukhala chifupi Nanu
Kukhala chifupi Nanu
Kukhala chifupi Nanu
Mmh mmh mmh
Mmh mmh mmh
Mmh mmh mmh
Mmh mmh mhh
Mmh mmh mmh
Mhh mmh mmh
Yeah, fupi Nanu

Поcмотреть все песни артиста

Sanatçının diğer albümleri

Benzer Sanatçılar