(Braxxy on the board)
Yah
Ya achina Seven adah
Ambuye amatikonda (yah)
Mulungu amatikonda (yah)
Chauta amatikonda (yah)
Ambuye amatikonda (yah)
Amatidzutsa tikagwa
Amatichilitsa tikadwala
Timuyimbire kuti izi 'pitilire
Ambuye amakonda aliyense
Mphepo imapeza aliyense
Mvula imagwera denga la aliyense
Dzuwa limapeza aliyense (yah)
Onani munthu, onani mbuzi, ona chi nkhuku, mwanapiye, khwiyo
Onani dzuwa, onani mwezi, chiphariwari kha-kha-kha-kha-khrr
Analenga zonsezi (yah)
Analenga nyanjazi (yah)
Analenga nyamazi (yah)
Analenga chambachi (yah)
Ngakhale mdima ungakure bwanji pa dziko lapansi kunja kumachabe
Ngakhale mvula ingavumbe bwanji pa dziko lapansi nyerere sizimfa
Analenga manyazi (yah)
Analenga nsanjezi (yah)
Analenga nkhawazi (yah)
Analenga imfayi (yah)
Analenga chisoni (yah)
Analenga misozi (yah)
Analenga chikondi (yah)
Analenga mtendere (yah)
Analenga Satana (yah)
Anthu m'matsapana (yah)
Anthu m'mangophana (yah)
Ana a Jah Jah wa (phrr)
Ambuye amatikonda (yah)
Mulungu amatikonda (yah)
Chauta amatikonda (yah)
Ambuye amatikonda (yah)
Amatidzutsa tikagwa (yeah, yeah)
Amatichilitsa tikadwala (yah, yah)
Timuyimbire kuti izi 'pitilire
Yah, yah
Yah, yah
Yah, yah
Yah, yah
Yah-yah
Yah-yah
Yah-yah
Yah-yah
Chopangidwa pa dziko lapansi
Chimathela pa dziko lapansi
Nkango Wayuda sangalore
Mpaka tsiku lina tizayimba
Mtendere (yah), mtendere (yah), pa dziko lapansi (yah)
Yesu ndi Mfumu yathu, ndi Mfumu ya mtendere (oh my God, oh my God, oh my God)
Mtendere (yah), mtendere (yah), pa dziko lapansi (yah, yah)
Yesu ndi mfumu yathu, ndi mfumu ya mtendere, eh (oh my God, oh my God, oh my God)
(Yah, yah)
(It's Simiya on the beat)
Поcмотреть все песни артиста
Sanatçının diğer albümleri