Kishore Kumar Hits

Quest MW - Dalitso şarkı sözleri

Sanatçı: Quest MW

albüm: Dalitso


(Okay)
Eya
Ukakhala pa mpata, mpata
Ukumbukire uko wachoka, 'choka
Ukakhala pa mpata, mpata
Ukumbukire uko wachoka, 'choka
Uzaziwa ndiwe blessing
Ndine dalitso
Ndine dalitso
Ndine dalitso
Ndine dalitso
Ndine dalitso
Ndine dalitso
Ndine dalitso
Ndine dalitso
Yeah, huh
Tikuchokera kutali (kutali)
Ku nkhondo ngati asilikali (Msilikali)
Ay, taponyeredwa miyala (miyala)
Kuti tidutse tinakakamira (kakamira)
Koma tapulumuka mu njira zodabwitsa (oh, no, no, no)
Kudutsapo ngati ndi pa Sapitwa (Sapitwa)
Oh my God, muli nane mission
Sinalakwe koma ndili prison
Koma chomwe sinayiwale ndine dali-
Mbuye wandichosera kutali
Njira yanga anandiyikira nyali
Nkona ndimayamika kumbali
Ukakhala pa mpata, mpata
Ukumbukire uko wachoka, 'choka
Ukakhala pa mpata, mpata, ay
Ukumbukire uko wachoka, 'choka
Uzaziwa ndiwe blessing
Ndine dalitso
Ndine dalitso
Ndine dalitso
Ndine dalitso
Ndine dalitso
Ndine dalitso
Ndine dalitso
Ndine dalitso
Ay, sanandiyiwalepo, sazandiyiwala
Amawonetsetsa ndi mpake nde ndizivala
Ndikadwala sindimwa mankhwala
Amawonesesa ndichire ine ndikadwala
Amandikonda
Kuyika trap pa manfana ondilonda (trap pa manfana ondilonda)
Samandizonda
Nikey Nikey boy zake tinachonga
Peace wazazitsa mu mtima
Ali ndi key, usasankhe wina
Ndeno please, usachitire mwina
Ndeno nthawi ina yake iwe
Ukakhala pa mpata, mpata
Ukumbukire uko wachoka, 'choka
Ukakhala pa mpata, mpata (ay)
Ukumbukire uko wachoka, 'choka
Uzaziwa ndiwe blessing
Ndine dalitso
Ndine dalitso
Ndine dalitso
Ndine dalitso
Ndine dalitso
Ndine dalitso
Ndine dalitso
Ndine dalitso

Поcмотреть все песни артиста

Sanatçının diğer albümleri

Benzer Sanatçılar