Koma boy's sizoonayi Henwood mhu mhu mhu Ase Trappy Mwana bad man Bad we de remix, (ah yah yah yah yah yah) You know waguan, (too ghetto too gutter) Its for da gin Yeah uh Ndukupalani mamba mafana Mumathamanga pakamwa Kukamba za ineyo Mpaka kutsamwa Munandidilitsapo panopa ndinazama Ukukayikira pita kafuse Anagama Lupanga pansi pa mphasa ndimagona pa bed Bawa chi penalty, ineyo ndi Mabedi Ati ndimakonda chani Ndawauza ma babe Ine ndichi Martse Mphwanga sungandivetse Hit after hit ngati mfana wa boxing Ndiku runner game, mafana you jogging Amkati ndine mfana uh, you joking Mukundi browser be, now you stalking Amkati ineyo ndi mfana Mabodza Chaka chino nde chi changa ine Mmanama Yah yah yah yah yah yah yah Amkati ineyo ndi mfana Mabodza Chaka chino nde chi changa ine Mmanama, (heeeee) Yah yah yah yah yah yah yah Amkati ndimayimba zong'aza Sinza hitter Ndine mfana osatha kucheza Sinzapita Ndizingokhalabe pompaja Ngati apaka glue Amkangondikambilana akakhala paka gulu Amvekele Czar uja nde samatha Sangavaye kulikose atha ngati ada aja Wangobwela kudzayesa zida akudoja Mumuona 2021 atagonja Mumanama mukuona zomwe ndikupangazi Ine ndikupanga dzina inu mukupanga zi Mukulimbana ndi beef, odi mchotse dalazi Ati Czar ndi wamisala, zopangira dala zi Yah, musama swethe nane Ndimadya thukuta langa, adad Nonsenu ndinu ana anga Ndimagetsa zi ma hit Ndine chiphinjo ndimabwera nzi ma verse Ndine mkulu wa mpingo Ndimatha kumenya nyimbo imodzi chaka chonse Komabe ndikunveka heavy chaka chonse Uona tima hater tanga tadaka tose Ti akazi tomwe mumafila ndaphaka tonse Mwana osatha kukwa, ndimayendachokhala Pano uwu handsome ndi mthumba Ndili ndizima looks Pano ndimadya bafa Mkana sindi spitter dirty Ndimadya rapper, kumusiya kulichete Amkati ineyo ndi mfana Mabodza Chaka chino nde chi changa ine Mmanama Yah yah yah yah yah yah yah Amkati ineyo ndi mfana Mabodza Chaka chino nde chi changa ine Mmanama, (yoo achina G-A) Yah yah yah yah yah yah yah, (yoo) Yoh rise up ghetto youth Nthawi yo huster asakupatse tchuthi Mfanawa amafuna ukhale m'musi Samasangalala uka riser ngati vu Koma ndiwafinya battery lo LIli full ndilisiya battery low Yo crew yanga siyama boss Ndi bad company ndupanga loss Heh ndungobwera ndima punch Fungo la usipe nanga udzimanilanji Ndine mfana ovaya heh Mfana woyaka too much Chifukwa ndi beef ndiya braz Ineyo mfana bodza Kapena amalota Samadziwa ndimasungiratu nyota uh Kungolimbika kunyoza Chilichose ndimagwira ndima conquer Mfuna Jane around mkazi wachikoka Kungomwyata silent osafooka Monday kungowona P-S but now you can't own her Chi babes ichichi ndichi deal Mood all day baby you can call it real Lilime lili swift i just shoot to kill Sindikusuntha inetu ndi mwini film Amkati ineyo ndi mfana Mabodza Chaka chino nde chi changa ine Mmanama Yah yah yah yah yah yah yah Amkati ineyo ndi mfana Mabodza Chaka chino nde chi changa ine Mmanama Yah yah yah yah yah yah yah Eh, i'm high as my feature fee You'll get hyped up off the greenery It's all thumbs koma it's never been visa V See we at the top stupid it's a different scenery I'm king resonant mob if you disagree I see no arm like a missing limb I've been stylish rapper shetin' calligraphy I'm rapping with fans every session is a meet and greet Ngini iyi yokha ndinazama Kutafuna ma beat oti mukhoza kutsamwa Mukumanga malamba ifeyo tinavaya Simudabwa ma guy ma collabo amandiswaya