Chariz Yeh Yeah yeah Yah Ukayamba geni ma guy akubwela ati nafeso Moyo okopela pamalawi wanyanya tisanamepo Ndikavalabo kutchena afuna avaleko Chinawatsalila mchiwanda chowonela mayeso Kopela chilichose kopela Akangoonela chilichose kopela Kopela chilichose kopela Akangoonela chilichose kopela Me and the gang we doing our own stuff To the top we raising we stop Mafana o hater Ali mu water Akunama akukamba Nena mabodza I'm tired of niggas telling me what to do I'm tired of niggas copying everything I do People follow even dropping out of school You copy cats do you really think that's cool Ku ding dong aliko Ku ghetto alikoso Ku ntchito aliko ma copy cut ayi nono Ukayamba geni ma guy akubwela ati nafeso Moyo okopela pamalawi wanyanya tisanamepo Ndikavalabo kutchena afuna avaleko Chinawatsalila mchiwanda chowonela mayeso Kopela chilichose kopela Akangoonela chilichose kopela Kopela chilichose kopela Akangoonela chilichose kopela Namenya cover nawo afuna amenye yawonso Kusiya hip hop umva kuti ayamba dancehall Sizophweka izi mphwanga iyi ndi mphatso Tili ndi dollar Ife timaphusha hustle Lemme see how you copy this I did a song with Emtee can you copy that Seven figures in the bank can you copy that All my friends super famous can you copy that Ku ding dong aliko Ku ghetto alikoso Ku ntchito aliko ma copy cut ayi nono Ukayamba geni ma guy akubwela ati nafeso Moyo okopela pamalawi wanyanya tisanamepo Ndikavalabo kutchena afuna avaleko Chinawatsalila mchiwanda chowonela mayeso Kopela chilichose kopela Akangoonela chilichose kopela Kopela chilichose kopela Akangoonela chilichose kopela