Kishore Kumar Hits

Hayze Engola - KANENENI şarkı sözleri

Sanatçı: Hayze Engola

albüm: KANENENI


Kaneneni kupolisi
Ngati sidzikuwazani
Window of opportunity
Inu kuseka makatani
They can say it to my face
Inu kuseli mukatani
Ife tima dropa hits
Iwo angotola nkhani
Kaneneni kupolisi
Ngati sidzikuwazani
Window of opportunity
Inu kuseka makatani
They can say it to my face
Inu kuseli mukatani
Ife tingo dropa hits
Iwo angotola nkhani
Kaneneni
Kaneneni (kaneneni, kaneneni)
Kaneneni
Kaneneni (kaneneni, kaneneni)
Usiku ndi usana
Ndingo hustle
Ndingopanga zaine
Sindikupanga za iwe
Ndingosanja daily
Kusaka kwacha
Matambala simachepa kwaine
Simachepa kwaine
Simachepa kwaine
Tidzipita eh tizinka
Bola ifeyo tikafike
Bola ifeyo tikafike
Bola ifeyo tikafike
Tilimo conquer
Chilichose izo nde musakaike
Izo nde musakaike
Izo nde musakaike
Kaneneni kupolisi
Ngati sidzikuwazani
Window of opportunity
Inu kuseka makatani
They can say it to my face
Inu kuseli mukatani
Ife tingo dropa hits
Iwo angotola nkhani
Kaneneni kupolisi
Ngati sidzikuwazani
Window of opportunity
Inu kuseka makatani
They can say it to my face
Inu kuseli mukatani
Ife tingo dropa hits
Iwo angotola nkhani
Kaneneni
Kaneneni (kaneneni, kaneneni)
Kaneneni
Kaneneni (kaneneni, kaneneni)
Panopa mudziziwa
Yachina Hayze
Ndiyamakani
Muzisintha ma sneaker
Mukamandilonda mapazi
Ndilitu ndi khama
Thukuta ndi magazi
Mukakwiya izo ndizanu
Izi ndizanziko lapansi
Dollar yo ikachuluka
Mdaniso akuchuluka
Ukalemba mmadzi
Nzovuta kufufuta
Sinagwadirepo munthu
Kuopa mabondo kusupuka
Sinagwadirepo munthu
Kuopa mabondo kusupuka
Kaneneni kupolisi
Ngati sidzikuwazani
Window of opportunity
Inu kuseka makatani
They can say it to my face
Inu kuseli mukatani
Ife tingo dropa hits
Iwo angotola nkhani
Kaneneni kupolisi
Ngati sidzikuwazani
Window of opportunity
Inu kuseka makatani
They can say it to my face
Inu kuseli mukatani
Ife tingo dropa hits
Iwo angotola nkhani
Kaneneni

Поcмотреть все песни артиста

Sanatçının diğer albümleri

Benzer Sanatçılar