Kishore Kumar Hits

Classick - Water şarkı sözleri

Sanatçı: Classick

albüm: Water


(Trappy on the beat)
M-O-D
Nfuna moyo
Nfuna moyo
Nfuna moyo, (zu zu zu)
Nfuna moyo
Ndufuna moyo, madzi a moyo, (zu zu zu)
Nfuna moyo
Tufuna moyo, madzi a moyo, (zu zu zu)
Moyo
Nfuna moyo, mfuna moyo, (zu zu zu)
Yeah uh uh
Its three o'clock up in the dawn and i just kept yawning, waiting for the morning hours
Walk up around like four o'clock to chase Lucifer, with that morning stars yeah
Realized dipping baptize is the reason why you keep falling
Thinking i am close to God and like i'm doing enough to understand my calling
So i call all of my homies, what's hunin' what's up
What's hunin' what's up
We shared a couple of stories
I told them enough, let's gp praise the Lord
Jesus is for everybody talk about it, all the people are highly favored
Understand your calling go to church and hear the rhythm
Whether you go balling making paper ey
I said patience, (oh no)
You don't have that, do you?
Are you ready? (God knows)
When you're ready all your dreams will come true
Are you ready or the pleasure of the things that you said you want
I asked, so when you see me go to church my senses just know don't ask, (that's)
Nfuna moyo
Nfuna moyo
Nfuna moyo, (zu zu zu)
Nfuna moyo
Ndufuna moyo, madzi a moyo, (zu zu zu)
Nfuna moyo
Tufuna moyo, madzi a moyo, (zu zu zu)
Moyo, (Achina G-A)
Nfuna moyo, mfuna moyo, (zu zu zu uh uh)
Yoh, ndidikira sinfooka heh
Sindililuza patient sine bad doctor
Yesu ndi legend kundikonda moyo ukoma
Ngakhale mu ghetto timakumana ndi zokhoma
Koma mavuto anga sali too deep
Chifukwa sinnalowe six feet
Mpaka satana akudabwa
Kuti koma mwana iwe si mfiti
Last night i didn't sleep
Satana amandinong'oneza koma ndine O-G
Nnamuwuza kuti real gee's don't go siphe
Dressed to kill koma i don't know, ngati ndi tchimo
Yesu ndi wa moyo if you don't know ndiwedi demon
Gattah Gattah tubwela kwanu
Madzi a moyo alipo?
Yeah, ndamu caller Piksy
Nfuna moyo
Nfuna moyo, madzi a moyo, (zu zu zu)
Nfuna moyo
Ndufuna moyo, madzi a moyo, (zu zu zu)
Nfuna moyo
Tufuna moyo, madzi a moyo, (zu zu zu)
Moyo
Nfuna moyo, mfuna moyo, (zu zu zu uh uh)
Tsiku lina tidzafa
Ngatinsukulapa disaster
Ena kulira ena kukhafa
Koma osamayiwala ku huster
Ukadiwa opanda dollar ndekuti mafanawa adzapanga suffer
Komano chimodzi mwa Yesu Khristu
Muli moyo wosatha
Ndikufuna moyo ngati ndinamira nde akundimenya ndi mchenga
Ndikufuna moyo mbuye wanga sinnamalize kugawa uthenga
Koma pena ndimadgwa ndidakali mwana nde ndikumayesera kuyenda
Nde ndikumadumpha kupewa kukwawa
Kuwopa chozemba
Kuthupi ndili healthy
Koma moyo wa uzimu nde ulipa drip
Koma mbuye analipira machimo anga onse mkusiyaka tip
He made me clean
Living life without Christ is risky
He paid the price, i'm not for sale
Sinful can miss me
Ndufuna moyo
Nfuna moyo, nfuna moyo, (yeah)
Nfuna moyo
Nfuna moyo, nfuna moyo
Mbuye wanga nfuna moyo oh
Nfuna moyo, mpatse moyo, (yeah)
Ndufuna moyo, (eish)
Nfuna moyo, mpatse moyo, (zu zu zu)
Yah uh uh

Поcмотреть все песни артиста

Sanatçının diğer albümleri

Benzer Sanatçılar