Kishore Kumar Hits

Theresa Phondo - Zambezi şarkı sözleri

Sanatçı: Theresa Phondo

albüm: Zambezi


Zoti kunja kuwala
Palibe angatsutse
Kuwona madzi mu khwawa oooh
Palibe angafunse
Kunja kuwala yeay yeah
Palibe angatsutse
Kuwona madzi mu khwawa oooh
Palibe angafunse
Ndendende ndi mmene
The way that I feel for you
Palibe chimene
I wouldn't do for you
Zoti ndimakukonda
Sizovuta kuwona
Chikondi changa pa iwe ndichokuya
Ndendende Zambezi
Awh yeah
Ndendende Zambezi
Ooohhhh
Ndendende Zambezi
Ayayayayaya ohhh
Ndendende Zambezi
Ayayayayaya oohhh
Dzuwa saalozelana
Zamumtima saauzilana
Koma zoti ine ndimakukonda iwe wekha
Palibe angatsutse
See my actions revealing
The way that I'm feeling
Na chikondi chokhachi palibepo oleletsa
Ndendende ndi mmene
The way that I feel for you
Palibe chimene
I wouldn't do for you
Zoti ndimakukonda
Sizovuta kuwona
Chikondi changa pa iwe ndichokuya
Ndendende Zambezi
Awh yeah
Ndendende Zambezi
Ooohhhh
Ndendende Zambezi
Ayayayayaya ohhh
Ndendende Zambezi
Ayayayayaya oohhh
Zoti ndimakukonda
Sizovuta kuwona
Chikondi changa pa iwe ndi chokuya
Ah yeah yeah yeah yeah yeah yeah
Ah yeah yeah yeah yeah yeah yeah
Ah yeah yeah yeah yeah yeah yeah
Ndendende Zambezi
Ah yeah yeah yeah yeah yeah yeah
Ah yeah yeah yeah yeah yeah yeah
Ah yeah yeah yeah yeah yeah yeah
Ndendende Zambezi

Поcмотреть все песни артиста

Sanatçının diğer albümleri

Benzer Sanatçılar