Chauta woo!
Tsiku loyamba lomwelija
Lomwelija
Limene munali kulenga ine
Ndilomwelo
Ndilomweli ndikuti beta munanchinja nkhope
Chauta woo!
Tsiku loyamba lomwelija
Lomwelija
Limene munali kulenga ine
Ndilomwelo
Ndilomweli ndikuti beta munanchinja nkhope
Nkhope yanga
Ndikhala ngati ndiliulira
Nkhope yanga
Ndikhala ngati ndiliupita or bwera,
Silidziwika bwino, i
Koma munakanchinja nkhope
Nkhope yanga
Ndikhala ngati ndiliulira
Nkhope yanga
Ndikhala ngati ndiliupita or bwera,
Silidziwika bwino, i
Koma munakanchinja nkhope
Oyang'ana (andiyesa Chitsilu yawa)
Oyang'ana (andiyesa wakuba ine)
Oyang'ana (andiyesa wolodza)
Chauta munakanchinja nkhope
Oyang'ana (andiyesa Chitsilu yawa)
Oyang'ana (andiyesa wakuba ine)
Oyang'ana (andiyesa wolodza)
Chauta ndaona bvuto
Поcмотреть все песни артиста
Sanatçının diğer albümleri