Kishore Kumar Hits

Lulu and mathumela band - Bwelera şarkı sözleri

Sanatçı: Lulu and mathumela band

albüm: Collection, Pt. 1


Ooh, oh-no
Ndinalinawe m'manja mwanga ne
Monga mbalame mu nchisa
Uli pafupi zinali zophweka kungonena kuti opusa
Izo ndimanena nditakhutane
Nsima yophikaso iwe
Honey mwapita, ndili ndekha
Sindipilira mubwelere
Chonde bwelera kunyumba
Mphavu ndilibe, nkhongono zi
Popanda iwe darling wanga
Mphavu ndilibe, nkhongono zi
Chonde bwelera kunyumba
Mphavu ndilibe, nkhongono zi
Popanda iwe darling wanga
Mphavu ndilibe, nkhongono zi
Hello-hello-hello, ukundimva kodi?
Sindikwanitsa chonde ubwere
Nzeru zanga zayima, thupi langa lathawa
Oh, please my sugar, ubwere
Uli pompha zimaphweka, you're the first out of all
Girl I'm so weak
Girl I need you
Uli pompha zimaphweka, you're the first out of all
Girl I'm so weak
Girl I need you
Chonde bwelera kunyumba
Mphavu ndilibe nkhongono zi
Popanda iwe darling wanga
Mphavu ndilibe nkhongono zi
Chonde bwelera kunyumba
Mphavu ndilibe, nkhongono zi
Popanda iwe darling wanga
Mphavu ndilibe, nkhongono zi
Lero lino ndawona kufunika kwako pamoyo wanga
Lero lino ndikulonjeza, sindidzaphwanyanso lonjezo langa
Ndidzakukonda mpakana imfa iwe, oh
Chonde bwelera kunyumba
Mphavu ndilibe, nkhongono zi
Popanda iwe darling wanga
Mphavu ndilibe, nkhongono zi
Chonde bwelera kunyumba
Mphavu ndilibe, nkhongono zi
Popanda iwe darling wanga
Mphavu ndilibe, nkhongono zi
Chonde bwelera kunyumba
Mphavu ndilibe, nkhongono zi
Popanda iwe darling wanga
Mphavu ndilibe, nkhongono zi

Поcмотреть все песни артиста

Sanatçının diğer albümleri

Benzer Sanatçılar