Udzindimvera udzindimvera pena
Udzindimvera udzindimvera baby
Udzindimvera udzindimvera pena
Udzindimvera udzindimvera baby
Palibe muthu amadziwa zonse
Zayekha anavika nsima madzi
Kuyenda awiri simatha
Zodziwa iwe nane singadziwe
Kulipo kumafa ndiludzu
Kulipo kumanka kutali
Kumakafufuza zeru katali
Okondeka wanga ndifunse
Ndidalile okondeka wanga
Ndiyang'ane okendeka wanga
Ndidalile okondeka wanga
Nditha kukhala opanda Ndalama
Koma undidali okondeka wanga
Undiyang'ane okondeka wanga
Udzindimvera udzindimvera pena
Udzindimvera udzindimvera baby
Udzindimvera udzindmivera pena
Udzindimvera udzindimvera baby
Ngati nkutukuka tidzatukuka tonse
Ku shayina ku shayina tonse
Udzindimvera udzindimvera baby
Dzatuka dzatuka tonse
Ku shayina ku shayina tonse
Udzindimvera udzindimvera baby
Usadzadziwe ntapita kale
Usazadzadziwe ine atanditenga
Mwendo wanga unali madzi
Nanga bwanji ndimafa ndi ludzu
Pena ndimavetsa kukula kwako
Tasiyana ndife a chimodzi
Koma ukadziyi lemekeza ndalama
Udzandisiya pa dzuwa
Ndidalile okondeka wanga
Ndiyang'ane okendeka wanga
Ndidalile okondeka wanga
Nditha kukhala opanda Ndalama
Koma undidali okondeka wanga
Undiyang'ane okondeka wanga
Udzindimvera udzindimvera pena
Udzindimvera udzindimvera baby
Udzindimvera udzindmivera pena
Udzindimvera udzindimvera baby
Ngati nkutukuka tidzatukuka tonse
Ku shayina ku shayina tonse
Udzindimvera udzindimvera baby
Dzatuka dzatuka tonse
Ku shayina ku shayina tonse
Udzindimvera udzindimvera baby
Поcмотреть все песни артиста
Sanatçının diğer albümleri