Kishore Kumar Hits

Ritaa - Nthawi şarkı sözleri

Sanatçı: Ritaa

albüm: Nthawi


M'dalitso wako udzatsika (Your blessing will come down)
Chisomo chake chidzatsika (His Grace will come down)
Nthawi yako idzafika (Your time will come)
Nyengo zako zidzasintha (Your seasons will change)
Chilichonse chomwe udzagwire (Everything you touch)
Chidzabala zipatso (Will bear fruit)
Chidzabala zipatso (Will bear fruit)
Thembelero lawo lidzakhala m'dalitso (Their curse will be your blessing)
Manyozo adzakhala matamando (Their insults will become praises)
Madando ako adzapeza mayankho (Your worries will be solved)
Nthawi, Nthawi idzafika (Time, time will come)
Nthawi idzafika (Time will come)
Nthawi idzafika (Tme will come)
Chimwemwe sindalama ai (Happiness is not money)
Usauzunze mtima (Do not trouble your heart)
Nthawi idzafika (Time will come)
Nthawi, Nthawi idzafika (Time, time will come)
Nthawi idzafika (Time will come)
Nthawi idzafika (Time will come)
Chimwemwe sindalama ai (Happiness is not money)
Usauzunze mtima (Do not trouble your heart)
Nthawi idzafika (Time will come)
Kupambana kosatha (Continuous victory)
Mtendere uzadza (Peace will come)
Mavuto adzatha, ingokhulupilira (No more troubles, just believe)
Sudzasowa kanthu (You will not lack)
Sudzanyozekanso (You will not be despised)
Sudzaderanso nkhawa (You will not worry)
Chilichonse olo usanapemphe (Anything, even if you do not ask)
Ambuye adzapatsa (God will Provide)
Ambuye adzapatsa (God will provide)
Thembelero lawo lidzakhala m'dalitso
Manyozo adzakhala matamando
Madando ako adzapeza mayankho
Oh, oh
Nthawi, Nthawi idzafika
Nthawi idzafika, Nthawi idzafika
Chimwemwe sindalama ai
Usauzunze mtima
Nthawi idzafika
Nthawi, Nthawi idzafika
Nthawi idzafika, Nthawi idzafika
Chimwemwe sindalama ai
Usauzunze mtima
Nthawi idzafika
Zonse umakhumba, umafuna (All that you want)
Osakakamiza... (Do not force it.)
Nthawi, Nthawi nthawi (Time, time, time)

Поcмотреть все песни артиста

Sanatçının diğer albümleri

Benzer Sanatçılar