Kishore Kumar Hits

Dr Namadingo - Telera şarkı sözleri

Sanatçı: Dr Namadingo

albüm: Telera


Na-na-na, Namadingo, oh
Sooner or later somebody is gonna say it, eh
Just a matter of time, yeah
Koma they'll surely say it, say it
Kapena mwina ndinene
Ndinene ndine
'Cause somebody has to
I see a lot of my sisters across the world on social media
Shaking it, kuligwedeza
Even on a picture sangangoyima bwinobwino
Koma atembenuke, anthu awone telera
Brother Dan ndiwokwatira koma Instagram sagona tulo
Brother Manzy sakupuma
Scrolling down and zooming in, awone telera
Alongo ena akumadziva kupelewera
Mpaka kusaka m'mankhwala abaye nawonso zitheke
Zili kuma WhatsApp status
Akumati happy customer
Kubaya kamodzo, mwezi umodzi, telera yabwera
Koma si galimoto lili lonse lifunika telera
Designer ku factory ndimomwe adali konzera
Musatsutsane ndi designer, sizimankondwetsa
Corolla adapanga kuti no-no-no telera
Mira no, no-no-no telera
Demio no telera
Isiyeni truck, it's okay, telera
Koma benz no, no-no-no telera
Beamer no-no-no, no-no, no-no-no telera
Isiyeni flat liner ikoke telera
Osatsutsana ndi designer
No-no-no telera

Поcмотреть все песни артиста

Sanatçının diğer albümleri

Benzer Sanatçılar