Kishore Kumar Hits

Driemo Mw - Mapiko şarkı sözleri

Sanatçı: Driemo Mw

albüm: Love letter

Driemo
Boy from the Kakalande
Mmmh, yeah
Nde ukati undisamale
Nkhawa zanga zonse uzisalaze
Ine Zimbabwe Iwe ukhale Harare
Umadziwa pondithobwanya
Maso ataona mtima unasunga
Mutu wanga natsimikiza ndamupeza wondisamala
Ndiwe chimwemwe changa
"Umabwera chaku mam'mawa"
Bwenzi la moyo wanga
Then I say
Ngati si iweyo, nde kulibenso wina
Ngati si ineyo, sungasankhenso wina
'Coz the way that I love you (way that i love)
The that you love me (the way that you love)
Love the way that you treat me
Ndiwe Ngelo opanda mapiko
Zonse mom'mo
Loving so more
Having you by my side ndi chisomo
Ndili ndi oyenda naye, mdima ukagwa
Ndili ndi ocheza naye, ndipo sindidera nkhawa
Eh komwe uli dzakhala konko
Wathamangitsa magazi a mphongo
Oh babe wandithetsa nkhongo
Sindingapitilire thera pompo, oh ineyo oh
Ngati si iweyo, nde kulibenso wina
Ngati si ineyo, sungasankhenso wina
'Coz the way that I love you (way that i love)
The that you love me (the way that you love)
Love the way that you treat me
Ndiwe Ngelo opanda mapiko
Mapiko, mapiko
Lovin' the way that you call me
Dad's, darling, baby ooh
Love me the way that nobody has ever
Ngati si iweyo, nde kulibenso wina
Ngati si ineyo, sungasankhenso wina
'Coz the way that I love you (way that i love)
The that you love me (the way that you love)
Love the way that you treat me
Ndiwe Ngelo opanda mapiko
Ngati si iweyo, nde kulibenso wina
Ngati si ineyo, sungasankhenso wina
'Coz the way that I love you (way that i love)
The that you love me (the way that you love)
Love the way that you treat me
Ndiwe Ngelo opanda mapiko

Поcмотреть все песни артиста

Sanatçının diğer albümleri

Benzer Sanatçılar