Oooh ooh ooh
It's Driemo
Yeah (mesa m'mati awa ndi anzanga, nzanga, nzanga)
Oooh yeah yeah yeah (Ine m'mati uyu ndi nzanga, nzanga, nzanga)
Anzanu aja lero
Anabwera mkumandiuza zinkhani (ooh ooh)
Nzako wina uja anabwera kuti ndimupatse plan (mmh)
Amandiyimbira phone
Ati wandisowa afuna andione
Ine bwanji ukupanga choncho?
Ati ndimakukonda kuposa Driemo yo
Mesa m'mati awa ndi anzanga
Nzanga, nzanga
Ine m'mati uyu ndi nzanga
Nzanga, nzanga
Amafuna akazi anga yeah
Atandilana oh
Amafuna amuna anga wa
Atandilanda oh
Ati chifukwa amayimba kuposa ine
Amatchena kuposa ine
Ati ndi okongola kuposa ine
Mkona anandithawa mwinamwake
Penapake ndimaseka
Ndikakhala ndekha
Mesa umkati ndine ndekha
Sumamvera za ena
Lero undinamiza chani (undinamiza chani)
Udiuza chani iwe
Mpaka ukagwidwa ndi nzanga (ukagwidwa ndi nzanga)
Kutengana ndi nzanga iwe
Mesa m'mati awa ndi anzanga
Nzanga, nzanga
Ine m'mati uyu ndi nzanga
Nzanga, nzanga
Amafuna akazi anga yeah
Atandilana oh
Amafuna amuna anga wa
Atandilanda oh nzanga
Pa ground patele
Zinthu zasolobana
Sungakhulupilire munthu
Sungamudalire munthu
Anzako omwewo
Nzako yemweyo
Amaganizira zina
Mtima wa nza m'tsidya lina ooh
Mesa m'mati awa ndi anzanga
Nzanga, nzanga
Ine m'mati uyu ndi nzanga
Nzanga, nzanga
Amafuna akazi anga yeah
Atandilana oh
Amafuna amuna anga wa
Atandilanda oh
Mesa m'mati awa ndi anzanga
Nzanga, nzanga
Ine m'mati uyu ndi nzanga
Nzanga, nzanga
Amafuna akazi anga yeah
Atandilana oh
Amafuna amuna anga wa
Atandilanda oh
Nzanga
Поcмотреть все песни артиста
Sanatçının diğer albümleri