It's Driemo
(Ndizapereke moyo wanga)
Oh, mtima uwupereke
Kwa ine ndiwutenge
Don't you worry about safety
Ndidzachengetera chengetera chengetera
I know mtima unaswekapo
You've been there unalirapo
Ululu mumtima kufikapo
Ukaganizira ganizira ganizira
Pa iwe ndilola ndipepere
Chikondi chisaperewere
Olo pa ground paterere I'll love you the same baby
Oh udzandifunse
Nkadzakuswera mtima udzandifunse
Kuti mwina compensation
Ndidzapereke moyo wanga
Oh, udzandifunse
Nkadzakuswera mtima udzandifunse
Kuti mwina compensation
Ndidzapereke moyo wanga
Oh, yeah yeah
Don't be scared to love me more
Zakale zapita it's me and you
Undiuze pomwe pali mantha ako
I know mtima umakana ukandiwunika
Umaona ngati aja anakunamiza koma
I wanna be your soldier
Your fighter, protector, defender
I just wanna be your friend for life oh
Oh, udzandifunse
Nkadzakuswera mtima udzandifunse
Kuti mwina compensation
Ndidzapereke moyo wanga
Oh, udzandifunse
Nkadzakuswera mtima udzandifunse
Kuti mwina compensation
Ndidzapereke moyo wanga
Oh, yeah yeah
Ooh, udzandifunse
Udzandifunse
Mwina compensation ndidzapereke moyo wanga
Oh, udzandifunse
Nkadzakuswera mtima udzandifunse
Kuti mwina compensation
Ndidzapereke moyo wanga
Oh, udzandifunse
Nkadzakuswera mtima udzandifunse
Kuti mwina compensation
Ndidzapereke moyo wanga
Oh, yeah yeah
Oh, udzandifunse
Udzandifunse
Mwina compensation ndidzapereke moyo wanga
Oh, udzandifunse
Udzandifunse
Mwina compensation ndidzapereke moyo wanga
Yeah, heh eeh
Поcмотреть все песни артиста
Sanatçının diğer albümleri