Kishore Kumar Hits

Driemo Mw - PANO şarkı sözleri

Sanatçı: Driemo Mw

albüm: PANO


It's Driemo ooh
Is this a joke?
Are you kidding me?
Utanthauza chani? zachuluka ndi nkhani
You're planning to leave me
Am I a fool?
For falling for you
Tadutsa muzambiri, tapangadi zambiri
Now you want to switch like that
Oh, kodi ndayipa pano
Ndakubowa pano
Zonse zija wandichititsa zikayipe pano?
Oh kodi ndayipa pano oh
Ndakubowa pano eh
Zonse zija unandiphunzitsa zikayipe lero?
Unandiyambitsa shisha, mowa mesa ndiwe?
Iwe na-ine muma club everyday
Lero ukuti khalidwe la banja mwa Ine mulibe
Kodi ndi game ya mtundu wanji you are playing?
Nde unkandisinthira? sinthiranji
Nde unkandisinthiranji? oh my God Ine
Fees yako itashupha ndinagulitsa munda Ine
Lero munagwidwa ndi shasha, ati ine ngwa kumunda oh
Koma izizi ndimkapanga chifukwa ndimasamala za ife
Ineyo ndinka blander kufuna kukusangalatsa iwe
How I wish I could go back (go back)
How I wish I could rewind
How I wish I could fall back (fall back)
But It's too late (too late)
Poti ndayipa pano (pano)
Ndakubowa pano (pano)
Zonse zija unandiphunzitsa zikayipe lero?
Unandiyambitsa shisha, mowa mesa ndiwe?
Iwe na-ine muma club everyday
Lero ukuti khalidwe la banja mwa Ine mulibe
Kodi ndi game ya mtundu wanji you are playing?
Nde unkandisinthira?
Zomwe mutandisiyile pano
Zomwe mudandiphunzitsa
Zomwe mutanditukwane nazo pano
Ndi zomwe mudandidziwitsa
Unandiyambitsa shisha, mowa mesa ndiwe?
Iwe na-ine muma club everyday
Lero ukuti khalidwe la banja mwa ine mulibe
Kodi ndi game ya mtundu wanji you are playing?
Nde unkandisinthira?
How I wish I could go back
How I wish I could rewind
Fall back, but It's too late (too late)

Поcмотреть все песни артиста

Sanatçının diğer albümleri

Benzer Sanatçılar